Mchewa kukanika kulakhula banzi ndi tea zili mkamwa
@juliusnjerengo2610
3 ай бұрын
Atumidwa awa ndi boma, their tongue say it all.
@bennihope3272
3 ай бұрын
Immigration yovunda ngati iyi. U mean the whole immigration printer imodzi. Where does Malawians money go which they pay for passports. Tell ur fellows in South Africa to stop robbing Malawians in South Africa by collecting money and fail to provide forms to government kamba koti ndalama zina mwasowetsa. Tsiku lina mudzaona polekera
@YoungMwacho
3 ай бұрын
Mkwezalamba waona mmene ndalama zimakomera, ku UNION kuja zinali zochepa panopa uli mu armpit ya Chakwela, be careful with your politics, Chilima has just lost his life. Do not trust MCP and Chakwela, ufela za eni. Mark my words. The love of money kills.
Zoti production yama passport ikuchitika Ku Lilongwe kokha dziko lonse lino mukuzidziwa?Kusonyeza kuti Ku Blantyre,Mangochi,Mzuzu ndi ma immigration ena,munatseka ❓❓
Timabungwe tina ngati zeru tilibe atolakhani musavutike nato. Ntchito timapereka kwamene akuyiziwa ena aziphuzira kwa iwo osati poti ndiwakwathu koma sakuziwa job. And wa itenk yo akudya ndi ndani Ndama poti mumadya inu opanda zeru Ife amalawi tikufuna ma passport osati company ikhale yazika ayi. Chakulu mzuzu blantyre ma passport azipangidwa osati tizigwada ku lilongwe ngati ndiyo fumu yazeru yokha
@IssahNsaliwa
3 ай бұрын
Useless government
@InnocentCcij
3 ай бұрын
😂😂😂 Chikuvuta ndichani kt mupange zotheka kt anthu asakhale Paukapolo bwanj please don't waste your time go on straight forward government sikuthandiza anthu 😢
This idiots I make my passport last year January 2023 until today she can't get it her passport including the eat my other money the say pocket money but the never give her passport
Mwangokura mitu koma opanda mfundo zomveka bwino zoti mkuwawuza a Malawi.... Useless meeting ever
@Eric-gb9ms
3 ай бұрын
Samalani nd amalawi beware of tomorrow please been long enough people's the don't get passport in time
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
3 ай бұрын
kodi bwanji vn siitheka ku fb comment .ndimafuna kutukwana.. company ya Nick chakwera thesani company yakale ibwerere
@michaelkallyz2425
3 ай бұрын
Ngati mwati mwatsitsa macosts, why are you failing to buy new printers nkuika kuno kuBlantyre ndikuMzuzu?
@giftchirwa9203
3 ай бұрын
Which phindu ma guys ma passport oti anthu akubwezedwa kunja.. palibe chanzeru...
@charlesadam7908
3 ай бұрын
Ñdinu agalu kwabasi mukanadziwa kuti ndalama timaipeza movutikira ine mpaka lero passport yanga sinatuluke ndinalipira December 26 last year ndiye zomwe mukuyankhula apa zopanda mutu nkomwe shupit
@lastonekaponya7675
3 ай бұрын
Koditu malawiyo akukanika ndiye kumangoti Malawi akukanika Ku printed mapasport zochitsiru Basi kungosokoneza sokoneza mubackira anthu opanda zeru
@maxwellmashon4897
3 ай бұрын
Tsopano Chakwera amatinamiza ife kuti anthu aupandu anapanga hack system ya ku Immigration chifukwa chani, ngati Chakwera amatinamiza, inuo mungatimamize motani? Vomelezani mwalephera
@AlexMthunziChimpeni
3 ай бұрын
Mwasisa kuti?passport ya normal ndi 150pin express ndi. 200 thousand kwacha.
Koma anthu inuyo mwagokula mitu achewa sindikunkhulupirira kuti kumeneko kuli azeru ayi ndinthu mabodza okhaokha chaka chamawa mukuchoka nonse mavoti tidzidzawerenga pompopompo pa
@YamikaniThoko
3 ай бұрын
Mungoyankhula za kachasu akuti kuopa kumagidwa zaziii osangoyankhula moveka kt chakwera atule pasi udindo bwanji
@EmmanuelZingwe-wf3cl
3 ай бұрын
Anthu inu mwatumidwa agalu inu.... Kod mukuwononga dziko ngat ana anu saona mavuto? Osamaikila kumbuyo makape 🤔🤔🤔😡
@Fanzo-h2l
3 ай бұрын
Zo0usa ma passport sakuyenera kupanga kumalawi ma passport a fage mbavaizi ma passport a Mankato chakwera ndi nduna zake alephera ma passport samapangira mnyumba ai agalu
@Fanzo-h2l
3 ай бұрын
Zo0usa ma passport sakuyenera kupanga kumalawi ma passport a fage mbavaizi ma passport a Mankato chakwera ndi nduna zake alephera ma passport samapangira mnyumba ai agalu
@madalitsophiri2373
3 ай бұрын
Eshiiii ine pano ndinapanga ya express last year until now kuli ziiii chonde tiganizireni tifa ndithu tikalandire chithandizo kuno ku mzuzu😢😢
@AlexMthunziChimpeni
3 ай бұрын
Zimawawa kulipira passport ya express akupanga passport ya normal.kuba kwake kwamtundu wanji a mcp.
@iangondwe6857
3 ай бұрын
All the best guys tikufunirani ntchito yabwino and the president himself all the best
@DigleDafter
3 ай бұрын
Zisiluzokhazokha izi zilibwari ya boma awa palibe chazeru chomwe tingakuvereni
Пікірлер: 211