Kodi ngakale akufuna asimanga wina aliyese kod ziku lovota asizamuopsesa munthu kapena asosayamba amanga Kaye mundu Kuti ukandivotere ine Ali ndichibwana nyamako yawoyo
@joaquegerman2250
16 күн бұрын
😅😅😅😅
@VincentMwala
13 күн бұрын
Auze anthu oipa
@user-lj7lm6ly7z
13 күн бұрын
Koma ndipoo ngati mukunama nthumazi ikwakwapula
@cynthiakananji1608
3 сағат бұрын
PhaaAAaaaaaaaaaaa
@masterchitabwino898
13 күн бұрын
Auze kkkkk
@daviechinthengaofficialcha7190
16 күн бұрын
Kkkkkkkkk
@JTUPHIRI
13 күн бұрын
Hahaha hahahaaaa!
@user-tl9xg4fg9x
12 күн бұрын
Akumanganitu boma lake lopengali
@joaquegerman2250
16 күн бұрын
Ndizoona chinachake chaola
@user-qn3be8ry4r
15 күн бұрын
Anyapalawa ankhawula a MCP
@FiquickTech
9 күн бұрын
Chamba
@Musa1828-l5d
5 күн бұрын
Chitsiru iwe
@hanifahmponda8711
15 күн бұрын
Kkkk awudze a MCP kuti aying'alula apa nsapulumuka 2025 wawutali kubela tsikuthekaso mwadzi wamunthu omvuta
@ClementinoAnerio
13 күн бұрын
Munthu oipa kwambili
@smartjilamu8026
15 күн бұрын
Zoonandi
@ChristinaLigomeka
15 күн бұрын
😂😂😂😂😂 Mwandiseketsa modzi wawo ndine a chilima sindikuwadziwa km tikuchoka tonse kuntcheu km ndadziwa bwino pangoziyi😂😂😂😂😂 ing'aluleni kampeni ikhala yandenge🤣🤣🤣🤣 ndimva kuwawa ndimfa yachilima ndi anthu 8 aja km Mwandiseketsa sakufuna koma ndye zawadera amcp km zinazi mukamapanga kumaunikila zithu ziwiri tikupangazi ubwino uchuluka kapena kuyipa kuchuluka km satana wakudodani achakwera ndi anthu anu muyisova 2025 is near😂😂😂😂😂😂
Пікірлер: 78