Chakwera ndi mbuzi yamuthu inu mwapanga chani mu 4 yrs ??? Ai lekani kunamiza amalawi
@TrysonChimenya4-fm8nt
14 күн бұрын
Malawi tikapusa tipitilira kuvutikabe President wanji wosapanga regret Mukamakavotera MCP kawiri zanu izo, Kodi bwanji sakutiuza percentage ya zomwe atipangila out of Promises????????? Time to vote for president based on region will no longer help us ....... Ine ndiye ayi Chakwera, Chilima akagwere ndi anthu onama zedi Komanso what we should know this is political battle, sangabwere poyera nkumatiuza kuti eya 2025 tizaluza that's why even those small small parties are promising that they will win come 2025. Uku nkulira kwanga ndatha ine wanu amalawi anzanga
@LovelyAzaleaFlower-uc8vr
14 күн бұрын
Ndipo you have said the truth anthu awawa mukut a MCP waaa God will give them a severe punishment
@samsonmtumbati4855
14 күн бұрын
Boma la mcp limatinamiza kwambiri kamuzu palibe chomwe adachita mdziko la Malawi chimene tikudziwa ndikuba ndalama za Malawi makolo athu amakagona kutchire chifukwa kamuzu amafuna misonkho ndiye kuti chiyani lero
Iwe ngodwala bwanji..... don't include kamuzu mukhani yako...he is the only guy that did good for Malawians ukafunse agogo ako...osati mbuzi zako Za dpp zo😂😂😂😂😂4get guys dpp will never come back muulamuliro
@bernardnyirenda7639
12 күн бұрын
K@@wisdom20mkango49
@LovelyBlini-cu3iu
14 күн бұрын
Mlungu atimenyela nkhondo bwana ngati mkudalira kuba ziwani ichi ku mwamba kuli mlungu
@ThokohKalonga-je9rx
14 күн бұрын
Kodi chifukwa chani amalawi timangopusisidwa apapa wbwera uyu ku blanttyre mukuombela manja ngati akupanga zinthu why!?
@user-zg7iw8kq4r
13 күн бұрын
Vuto dzikoli mbuli zachuluka
@user-oo1sx7fb4v
13 күн бұрын
Ndalama
@charleslimbani8590
13 күн бұрын
Ndiye muziwe kuti zokonda za inuyo c zokonda za awooo.....ngati inuyo mumakonda Dpp musayembekeze kuti awo akondanso Dpp ayiiii .....ngati mmaombera mmanja Peter ...panopa ena akuombera mmanja chakwera.....ngati mwagona ndi njara pa khomo panu musayembekezere kuti kwa Neba nakonso agona ndi njara .....umo ndi momwe moyo umakharira ......simungawapange anthu onse kuti akonde Dpp ......koma wanzeru amakwera Timu imene ikusogora pa ground nthawi zambiri yoluza .........
@AliSalimu-wl3vi
14 күн бұрын
Koma guys kod ku state house ku amasuta chamba eti nanga boza limeneli bwanji
@babranzima8120
14 күн бұрын
Akuzinamiza amenewo
@LovelyAzaleaFlower-uc8vr
14 күн бұрын
MCP ikuzinamiza Peter is already chosen to be president of MALAWI
@CliveNdalama
13 күн бұрын
😂😂😂😂
@VincentChikondano
14 күн бұрын
Stadium sinadzadze or half nde simungadabwe?
@user-gk3bb8dx1m
14 күн бұрын
Apm my vote
@user-nj4ob8jw6y
13 күн бұрын
Your president is another Bola Tinubu of Malawi, sorry he has pasted his sell by date, u can even ask Namalomba.
Makamaka chisilamAchakwera amadana nacho limodzi nd anthu akulilongwe,bas zingo khala zamutundu,tsopano msilam ndye ali paliponse,azichemwali anu onse anakwatiwapo ndi msilamu tili ndi anatu mwa kabudulamu, kuphiri la njudz,kwamasumba,ndye nkhondoyo ife tingo ona kucheedwa,kt tikuonetsen
@geoffreykankhomba
12 күн бұрын
Ovota ndi anthufe kulankhula uku its like ma vote muli nawo mnyumba mwanu ,sitinaiwale ñjala ,kukwera kwa zinthu kubvuta kwa chakudya ,kukwera kwa chimanga mpaka 60 000 zomwe sizinachitikepo mu History ya Malawi ,ziwani kuti anthu ada nanu kukhosi kuyambira ku primary school mpaka ku collage ,ma civil servants ndi Ena onse ,aphunzitsi ndi ena onse ,kufikira munthu wakumuzi sakufunanso kumva dzina la tonse alliance and MCP tionana September 2025 ndipamene mudzaziwe kuti Amalawi anatopa nanu
@patrickscott9086
13 күн бұрын
Ndizona tizivutikabe bas muziba ndalama muzilemba job aku banja lanu
@KondwaniJ.Nkhoma-wt5zo
13 күн бұрын
Awaso koma akodzera bulangete sanayanike. Ayiwala kuti usiku ukubweraso
@louischitete1076
13 күн бұрын
Chakwela my vote kulibe opikisana naye uyo ndi owina basi
@JonathanDube-vc5qp
10 күн бұрын
I support, chakwera is going to win❤
@giftjamali8204
13 күн бұрын
Muthu ukamati nkazi uyu ndimukwatila umakhapa kuti madongosolo onse ofunikira manja wapanga Apure akukunaminzani pls konzani nyumba yanu yokapumila
@user-jw5rx9ze8k
13 күн бұрын
Koma chakwera mwati ali ndi nzeru? Ndikuona ngati chomwe akuyankhula sakuchidziwa.
@ChifundoChingwalu
13 күн бұрын
Ngati tili ovota ndiiyeyo Sadzadzitha
@EmmanuelGasiten-fo5dr
14 күн бұрын
Apule kuyesera kubayibitsa anthu ku Kamuzu Stadium, eti anthu kumangoyang'ana osabwezera kkkkkk! Koma m'Malawi anakonza ndithu.
@JackMvura-ik2td
14 күн бұрын
Sanje akulu ndinu afiti eti mumadya matewera kwanu eti demeti or pitala angafike gulu limeneli mbuzi
A malawi apitako kut akalandile ndrama kenako azibwerako kma zot mungawine nde izo lekan ndithu
@Malawinews1
14 күн бұрын
Cant you memorize the script and present as you not just reading...
@MwambakuluKamwambasa
14 күн бұрын
Am a boy who belong to both two sides Lomwe and Chemwa because my dad from kasungu in Santhe and mom in thyolo Thomas .u like it or not .am a solution.
Wina aliyense amakondedwa ndi Mulungu. Ndiye osamanyoza mtsogoleri wathu. Ngati inu si a malawi samukani koma ine sindikuona chomwe walakwa pa zomwe wayankhulazi. Tisiye kusankhana mitundu ndipo uthenga uwu wa achakwela ndiowona ndinso omanga dziko.
@user-rl8xs2kf1o
14 күн бұрын
Kodi Ali ku kapeni 😂 ayiwala zomwe apitira mbuzi za anthu
@user-cq1wv9nq4y
14 күн бұрын
Aaaaa ine mmene ndanvera ma speech awo kumeneku nduona kuti uyu unali mnsonkhano wa ndale wa mcp not mwambo okumbukila Kamuzu asamatinamizepo apa olo aja akuti achimwendo aja kulakhula kwanji kumenekuja ati akutchula Peter Munthalika ati sangatenge boma aaaaa zugwirizana chani ndi mwambo okumbukila malemu Kamuzu??? Eeeee koma guys ku Malawi mmm ayi zikomo
@EmanuelMuotcha
14 күн бұрын
Masapota amanoma ukuona ngati amabwelela iwe galu wamunthu simasapota a mcp ayi
@user-du9qs4tb6u
14 күн бұрын
Akufuna kubela agalu awa
@DicksonBinali
14 күн бұрын
Namapwala iwe ntchende lako boma lake liti utapitilizelo mapwala
@user-vm7iz6oz6r
14 күн бұрын
Wandikweza bp sindikwanisa kumaliza video iyi , zausiru
@mussahkachere2332
14 күн бұрын
Kom amalawi nd anthu onvesa chison kwambil 😂😂😂..anthu tikuvutika km still kuiimbila mmanja zinthu zopanda sogolo..
@preciousthafungaunje6631
14 күн бұрын
Osaiwala kut amalawi Fe Tu tangofuma kumudyela munthu kma awa antha
@Eric-gb9ms
14 күн бұрын
Eti makamaka azimayi chosecho usiku azikagona nd njala
@Hastings-on9is
14 күн бұрын
Sindikuziwa kut anthufe timaganiza Chan,, mpaka kululutira garu ija koma😢
Ife siana kuti tizinamidzidwa zopusa ngati izi. After all panopa m'Malawi wina aliyense wavota kale pano. Development starts with basic needs. Nde dziko litukuka bwanji highly expensive Life this?
@patrickmenyauti4876
14 күн бұрын
Awa ndi achisiru ndithu
@user-lf6qf2tw5o
13 күн бұрын
Ukufuna uzabele mavote Garu iww
@MadalitsoKondwan
13 күн бұрын
Aziwona asiyeni azachita manyanz awa
@robertnambazo9936
14 күн бұрын
Mr Pule mwapanga chani choyanjanisa kuposa Kuba ndi katangale nzikomu njala thoo muzikomu
@user-xs3nj1es1r
14 күн бұрын
Peter Mutharika awinaso🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@user-ce6hy6tp7e
14 күн бұрын
Amalawi ndnu anthu opusa kwambiri mumangovokera zili zonse chakwera ndi munthu oti ali ndi phindu mpaka kumuombera mmanja zisiru inu ine chakwera amandinyasa ndpo kwambiri mwana wasatana ameneyo
Пікірлер: 535