Dr Chilima your legacy shall live on until children yet unborn will learn about you our fearless young leader . The VP who was always there for Malawians. God be with The Family, the Party and all friends.
@LerinaKatuli
10 күн бұрын
We all crying. But we put everything in the hands of the Lord.
@kingsleychatha7492
10 күн бұрын
Bp yanga ikanali yokwera, komanso pena zikungooneka ngati maloto
@MadiIdrissa-zt3rv
10 күн бұрын
Kuno kwathu ku Malawi kulibe anthu akatswiri amene amadziwa za kufufuza za ngozi ya ndenge pamafunika akatswiri eni eni from the manufacturer in Germany and engineers a Malawi Civil aviation ndi a MDF chonde asagwire kulibe aircraft accident investigators chonde. Ine retired officer ku Malawi Civil Aviation.
@alfredbanda1693
10 күн бұрын
Palibe chomwe mukudziwa ingokhala mphee. NTSB imapanga ndege
@FranklinNdovi
10 күн бұрын
Witches and wizards also cry for the deceased they have bewitched. But those are called the sons and daughters of Lucifer who hate the light which defeats the darkness of the world. Hallelujah, son of David have mercy on our country Malawi. We humbly pray that power of resurrection of Jesus Christ reign over our nation so that there should be peace and love from God.
@AnusaNkhoma
10 күн бұрын
Kuyankhula kwamai kaliati uyuu ndi mamuna
@samuelmchekachilenje1259
10 күн бұрын
All press briefings by UTM, why is the Vice president of UTM missing? May our God keep the soul of the departed Right Honourable Dr Chilima and the 9 other souls rest in peace.
@user-yh7tt3em5w
10 күн бұрын
Alliance tinapanga ija inali mistake ndikuona choncho tikanangomvomereza zativuta then titzapikisani nawo mu 2025 but too late Aaaaaaa zandikwana zinthu Munthu sangafase choncho ayi why Koma 😭😭😭😭😭😭💔💔💔💔💔🙌
@OdettaLowrence
10 күн бұрын
Akweni mwayakhula zoonadi zioneka, wakupha chakwera main point, tisaope ndango, alula basi ishiiii
@sheila5812
8 күн бұрын
Akweni akhale president wa UTM
@catherinechirwa8096
10 күн бұрын
Manganya naye akudabwitsa zochitika zake coz he is not there
@JackElias-ty2tt
10 күн бұрын
Kaliati kulankhula mawu a mphamvu
@user-zc1mg5lj7p
10 күн бұрын
Mitima ya tonse a malawi osati a utm okha ikuwawa mosafuna kunama chakwera asewera game yolakwika
@HaliJana
10 күн бұрын
KUMALILOKO CHAKWERA ASAFIKEKE NGATI ALI NDI UMUNTHU NDI GALU WACHABECHABE
@HarrisWipa
9 күн бұрын
Amalawi we always say zonse adziwa ndambuye ask yourself why God gave mphanvu manja miyende kuphatikizans ubongo,,,it's because He knew kut pazakhala zinthu Zina zkyenera kut tithane nazo tokha this is the time to take the action osamangoti ambuye adziwa zonse what's that
@paulmaseko4245
9 күн бұрын
Good idea and I wish Chakwela awone zowawa pamodzi ndi crew yake kufikila avomeleze kuti malawi wawawidwadi mtima ndi kuphedwa kwa Chilima
Mai kaliyati nkhani chonde choona chidziwike ndithu apa mmmmm kuyakhula kwake kukuvuta ndithu koma dziwani kuti padziko lapasi palibe chisisi afiti,asatanic ose azaululika poyela osalolera kuti mukhale chete pankhani imeneyi yesesani kupeza akadaulo odziwa ntchito yakafukufuku tidziwe choona ndithu
@ShekelengDavid
10 күн бұрын
No secret under the sun......plis ziulululika.....
@user-gm6ig2fm8y
10 күн бұрын
Vuto Malawi ndife ogona siochangamuka ngati mayiko ena kafukufuku weniweni alipo koma ena akuwopa kubwela poyela kuwopa kumphedwa anthu eni eni monga wankulu wa asilikali ndi apulezedenti ndi amene akuziwa chilungamo
@SheilaMabvula
9 күн бұрын
If i know Dr Chilima well even his soul cannot let the wicked walk freely
Km kumeneko muti mukaona Apitad kapena ine izi zikundichitikila kumaloto Mwina simnadzuke kapena Mwatiliza ife Amayooooo 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 Ndege Astikali ku Israel Atisiila misoz ife Amayoooo ine chilima
ine ndine okhuzidwa kwambili and mu malawi sitizapezanso msogoleli wa maso phenya ngati uyu and achakwela anenepo zoona pa khani ya infa ya a chilima and palibeso wina akuziwa za infa yake choti muziwe ndichoti chilima wapita ndi voti yanga sindizavotaso .
@user-xd1cm7tm7t
10 күн бұрын
Kaliat iwe ukupeleka fundo zokwima kuposa azibambot boma likunjenjemela nawe
@johnchipeta-vo4wd
9 күн бұрын
The vice President of UTM isn't visible!!! Where's Michael Usi? What's not happening?
Пікірлер: 178