Walowa dziko litavunda kale palibe chingasithe apa😢😢
@AlfredNazombe-me2ly
5 күн бұрын
Kod awa atatu ndiamene ali oziwa kwambiri amangokhala pamenepa bwanji
@user-vu4cz1mt4f
5 күн бұрын
Tili nchisoni chanji,anagawana zovala zanga yesu anatero
@user-bl6km6kx7n
4 күн бұрын
Mabwana chonde kuyamikila tiyamikile koma kod chikalidwe chathu monga amalawi chimati chani munthu akafa plz timakukulupililani
@user-ve2ts3yr2n
5 күн бұрын
Ndipo mukhalisepo atumwi inu.....aaaa ma compassion aanthu mpaka zaka peletu ati sanasayinile.....
@AlfredNazombe-me2ly
5 күн бұрын
They think that this TTV it's belong to them kom kumakhala bwn ndi anzanu zatsogolo lamunth amaziwa ndi Mulungu
@user-wx1jt5fd2j
5 күн бұрын
Ndi andale ochepa amavomereza kuti chiweluzo chiliko ndi chifukwa chake samasamala za anthu Ena ngakhale akubvutika bora iwo zawo zikuyenda koma mulungu ndi oweluza olungama
@user-co3wr3rn4h
5 күн бұрын
Manganya ndi ka yudasi kakafupi kwambili fiti kapha, zake chilima
@MustafaAbdullah-pb5zv
4 күн бұрын
Powerful message
@corretabanda7685
5 күн бұрын
Ine sanandipeze speech yawo nsaname
@ClementJacob-sd8lf
2 күн бұрын
Sugar k200 Lifeboy soap k50 nthochi 20 t, zibwelele kwa d.r banda ngati sizitelo nde kutinamizako ife sitifuna ndale
@EsnartMartin
5 күн бұрын
Ma guy inuyo simuli serious ndale zakulowani
@yusufbakali
4 күн бұрын
❤ Manganya ndiyekhayo maso a malawi
@josephhchimpepa8753
5 күн бұрын
That's a good discussion! Those who have ears have heard something!
We are waiting incompetent inquiry Poor leadership Not following the democratic values Remember next year is just around the corner Things are not working on the ground Guys we need a servant leader
Mudya nyemba amayiwala, koma mudya makoko sayiwala
@LovemoreTaulo-yj3pj
5 күн бұрын
Times mcp tv mbuyomu inali times ya bwino km pano anawadyesa Baz awa
@adibwekumz3085
2 күн бұрын
That's illegal. Kupusa
@homeremedys3748
5 күн бұрын
Akufuna Aphe Born Kalindo then APM, chenjerani nayoni boma ili zinali kokambilana dzulo
@ZungeniBanet
5 күн бұрын
Inu chupiti
@SamukLungu-zg7fl
5 күн бұрын
Ausi kaya ndi usi wamutengo utiwo koma mumbari yopha chirima arimomo koma nawo apitabe basi
@user-nw6ie3xx8b
5 күн бұрын
Wishing you the best , help chakwera he is the man of God
@MichaelWilliamsNyirenda
5 күн бұрын
😅 killing man
@user-gs7wc3nx3q
5 күн бұрын
Iya mapazi anu
@dymonleven7571
5 күн бұрын
Abambo asikono kumeneko zalowa chibwana ndithu 😊
@ykzt
4 күн бұрын
Kod pali chodyadira pamenepo anthu inu
@ChrissySasenga
3 күн бұрын
Chilima anali dolo simukunama
@AlexKaunda-ny2eg
5 күн бұрын
Agalu atatuwaso atinyasa machende anu
@wypatrickdakankhoma9655
5 күн бұрын
Mwakwera m c p😢
@PatrickMailos
5 күн бұрын
I disappointed MCP
@Yungjoe786
5 күн бұрын
Pachoka nzako palidi Malo...
@RABSONSIKELO
5 күн бұрын
Moyodi ndi pelete
@MAYGOSPELALBUMSChawawa
5 күн бұрын
Don't take malawian as stupid because the president has got powers to make decisions like on this situation to change the decision because you can see when did we did the barial for Chilima and today you're busy enjoying with the post of vice president shamm on you mr. President and your vice president
@AlfredNazombe-me2ly
5 күн бұрын
I hate nyana these guys bcoz even they isolate Jona Pankuku every program they put Jona at last sit why and they use to cat him word on the mouth when ever he is speaking just wash 5 kwagwanji and hot current u will agree with me
@polesanamakwenda6932
5 күн бұрын
Kkkkkk
@user-nf3ik3ff6y
5 күн бұрын
Dziko latha
@IssaJohn-cb8vn
5 күн бұрын
This stupid radio this days we must stop listening and trust
MCP yamagazi yanuyo ngakhale itachita zabwino komabe mbiri yake ndiyamagazi basi
@SaidiMbawa-st6bj
5 күн бұрын
Dpp so ndi yamagazi ndiye musathe mawu boma ndi Boma
@tasmania527
5 күн бұрын
Ndipo DPP yinathiphela abale athu 20 ku Mzuzu mu 2011. Yinapha Chasowa, Njaunju, ndi ma membala a UTM ku Lilongwe; kodi amenewo si magazi a anthu? Kodi anthu onsewa ophedwa ndi DPP anali nkhumba? Nde musamalankhule kuti MCP yamagazi ngati muli ndi umboni- DPP umboni ulipo.
@MaryNyirenda-nq3mh
5 күн бұрын
Kod anthu mulimbalibe ya MCP yomweyo uhuuuu bola zipani zina osat MCP yakupha
@tasmania527
5 күн бұрын
Za zii. I would rather support MCP than family parties of killers like DPP or UDF
@kingsleyhopematchaya5184
5 күн бұрын
Nanga popeza yakhala mcp yokha chipani cha phavu nanga muthu wa zaka 92 angaganize zulu zinatha tiyenazoni bola mukavote katatu aliyese koma kamodzi aaa mcp ikudutsa
@AlexAlick-bx9by
5 күн бұрын
Times it's mcp TV
@MOOSANOWAH184
5 күн бұрын
Kuyambila liti?
@JafaliAkimu-ll1bf
5 күн бұрын
boma lolamula ndi chigawenga
@IssacMateyo
5 күн бұрын
Palibe ndipo ine ndiye ndakodwa kwambili ausi vice 🔥🔥
@IssacMateyo
5 күн бұрын
Palibe ndipo ine ndiye ndakodwa kwambili ausi vice 🔥🔥
Пікірлер: 89