Munthu akulephela kuyenda uyo kkkk akasegule mega fam uko ndalama anaba zija
@thulanimpphiri6873
11 күн бұрын
Kodi azimayiwo ndiokwatiwa kapena anakwatiwa ndizipani. Chifukwa mukazi wanthu wazeru sangavinire mutsogoleri munawonapo mkazi achakwera akuvina ine ndi banja langa sitingapange zopusa kuvinira mtsogoleri ndindani? Bola ndifwe ndiwumphawe wamga zopusa sindingavine nawo olemera ali ndi ana awo koma bwanji savina
@user-uc1pd1tc2x
8 күн бұрын
Anthu ulenelero wadziko la pansi 😢😢😢
@user-uc1pd1tc2x
8 күн бұрын
Koma umphawi wathuwu ndimavuto mmmm
@user-oc9vl9xz8e
7 күн бұрын
Azibambo osowa zochita amenewa
@user-uc1pd1tc2x
8 күн бұрын
Nyau zopanda mnzeru izi
@MiracleMalichi
7 күн бұрын
Kodi andale otchona atulkukira pa mw mmesa joice Banda anali ku Johns ndiye 😂😂😂😂😂
@user-lf6qf2tw5o
10 күн бұрын
Azimai polan Moto mpaka pa hanifa
@mirriamwilliam-nq9wg
10 күн бұрын
Amalawi kusowa zochitatu ukuuu,,, nwayamba kunkhuta August muyambe kulira ndi njala mwaiwala kale
Пікірлер: 22