Madala mulungu akudaliseni ndi mau omwe mwawagawira anthu onse mudziko lathu la Malawi. Mwalankhula bwino mopanda manthu, ndipo anthu ngati inu ndi amene akusowekela kuti dziko lathu liphulidwe mu msinga za moto. Well done papa
@AjeliMw
21 күн бұрын
Perfect said but pomuika Bon Kalindo mu gulu limenelo nde mukulakwitsa Bon Kalindo ndi president wa amphawife we proud of him
@meganabigail-ye7fw
21 күн бұрын
Walakwisa kwambiri
@user-un6mw5wm3x
22 күн бұрын
Very good kumeneko nde kulankhula, Auzen avesese bwino bwino anthu wa
@user-cy7gd1go6y
22 күн бұрын
Fire 🔥 my fada
@WisikiBlack-gj4gu
22 күн бұрын
Born kalindo anapepesa mukululukileni, koma pachiyambi anasokonekela, koma anatutumuka athu atataisa kale, koma uyuyu uyu aaaaa tayeni akufuna kusokoneza wabhaletayu ndimagalaziyu,,
@KenedyBizwick-lh8bu
22 күн бұрын
Aaa akulu mwapalatu pamenepo kalindo anapepesa ndipo amalankhula zonveka zonzeka mwinatso kupotsa inuyo the DC nd katundu omanga ndimalamba
@user-ln3zx6wo4w
12 күн бұрын
Kumpoto nkwachilima ndi afod not dpp nde 50+1 mukaitengakut
Ameneyu atisamale mambo chitsiru cha munthu kuchoka ku Zambia uko
@yusufuadamu5476
17 күн бұрын
Komano mukudziwa kuti Bon kalindo adapepesa kwa A Malawi pachimene chidachitikaAnd We all know that no One is perfect,Freedom fighter Mr Bon kalindo is trying His Best.
@YakiKandeu
20 күн бұрын
Malawi it's for us let's stand en fight for our rights we nid to make malawi better dats it guys malawi yapoila hvy
@GolaMwanza-oi3oj
22 күн бұрын
Zingayambe kuyiwalika
@IMEDISHAMILA
21 күн бұрын
Kutokota kwabwino kwambli big man
@duncainjimmy
22 күн бұрын
Komano Bon kalindo as omenyera ufulu sakuyenera kuimilira chipani komano aziyima pa choonadi . Kalindo is the last man standing indeed. Ndangokonza pa Bon kalindo kuti aime poyera ndikulowa DPP/UDF mm ndizomwetu Mtambo wathela zolowa chipani
@user-ve4yl1gq8e
21 күн бұрын
Mwalankhula bwino koma koma pomutchula boni kalindo mwalakwitsa kozi iye anabwera poela nkupepesa ntundu wa amalawi ndipo amalawi anamukhululukila nchifukwa mukuona kut akalindo akalankhula amalawi akumawamvela ndi chidwi end next time osazanyozaso kalindo
@user-xd1cm7tm7t
22 күн бұрын
The dc trusted for us
@andrewnjawala
21 күн бұрын
Nice speech but kalindo anapepesa, so let's fight together
@user-vh1cq5gs5u
21 күн бұрын
Mdala uyu kwamuvuta mkunvetsetsa born kalindo amadzudzula ndipo sakunama born kalindo
@sparkdymon3429
18 күн бұрын
Muthu mulala wayowoya 200 %
@user-jw5rx9ze8k
21 күн бұрын
Bon kalindo yekhayo, muchotsemoni abale.
@HfamilyMw
18 күн бұрын
Kweeee
@IsaiahPaul-xf3jg
16 күн бұрын
Kulakhula mwanzeru
@JacobKapange
21 күн бұрын
Awa ndi a DPP. akumva kuwawa mmene anachoseledwa muboma ndipo simuzawina wina even come 2025
@timothymhone2340
22 күн бұрын
Tangolankhulani zoti mzapange mkawina zanzeru please 25yrs Mndale koma zaziii
@Mike-du7zt
21 күн бұрын
Eti ayise
@GraceLimani-zw7dx
22 күн бұрын
Mulungu si Jacob a ziona asiyeni atase amenewo adzaithawa malawi
@user-zq5ob7xz4l
22 күн бұрын
Bon kalindooooooo
@DONNEXKhama-bk1gy
20 күн бұрын
Yes your right but only kalindo Leave him he is innocent man
KZitem yaphweka, munthu wandale kuyankhula zopepera chonchi, muzamanga mtambo, iwe ndi wa police? Kudzichemerera koma kuyankhula zopusa, paja umbuliwu ndi andale omwe eti? Tangoperekani maganizo anu osutsana ndi mtambo ndi andale koma akhale maganizo olongosoka osati zopusa ngati izi.
Uchisiru wanu ndiumene unakutulutsani dpp and udf ure not holy ndipo am promising yu guys simuzawina unless muzasinthe kachitidwe kanu
@WilfredMathews-yl6ij
20 күн бұрын
Mdala iwey according to your speech tikuziwa kut ndiwazipani ziwiri watchulazo km born kalindo musiye pliz leave that Guy alone pliz,fundo zako ndizabwn ndithu km panga zako
@user-mj3ms4jt3b
22 күн бұрын
Uyu ndichitsilu kwambiri, ife ngati amalawi amaliseche akumwera sitikuwanaso iyeyu afune asafune tonse alliance iwinaso. Padziko lonse lapansi tikati zitukuko ndikumanga maziko atsogolo la mawa. Galu iweyo tanena zomwe amaliseche akumwera ndi DPP ndi UDF zomwe anachita zomwe zikupindulila amalawi lero lino kwa zaka 6 zomwe analamulira amalisewo ukuwatamawo. Kumangoyika Miyala basi ndalamazo mkumagawa kwa anthu akumwera chimenecho ndi chitukuko? Mbombela university ndalama aGalu inu adpp ndi UDF mwakhala mukutenga kwa zaka 6 zonse pa budget yaboma koma mpaka tinakuchotsani m'boma musanamange mbombela university. Sizokhazo ndizambiri ndipo iwalani zoti muzalowaso m'bale aGalu inu loko MEC chair person akatakhala mwana wa amaliseche akumwera simungawine chisankho. Anthu oipa inu kwambiri akudya anthu ndi mafupa omwe
@ZelinaKisswell
22 күн бұрын
😂😂😂 agalu kusekana zikundo , chakwera wako wapanga chani apart from devaluation, kukwera Kwa zinthu ndi corruption. Zogawa ndalamazo Aku Lilongwe kukasiya Mesa akumalandira ma 700 thousand pezan zina zolankhula akulu
@joelmakwinjakambalame9652
22 күн бұрын
Ameneyudi ndi ofoyila sangaone anthu mmene akangulula njinga zamoto ndi mmidzi momwe. Kabaza sanayamba nthawi ya DPP. Pano mumuuze akayime mmaboda akaowone ndi njinga zamoto zingati or zakapalasa zikulowa
@user-dw9zi6bo3o
16 күн бұрын
I doubt the claiming here in that he is a seasoned and shrewd politician. Sound knows nothing other than being a blind royalists. He is a just a supporter of DPP and UDF as he voluntarily confesses herein. Cant understand what he is up to begging for DPP and UDF sympathy. He thinks he can advise Nankhumwa yet he needs advice himself. Nankhumwa will shame them by dividing the DPP vote. He understands very little about the Nankhumwa effect, talking about 'alibe ndarama zopangila' ma branch, what a warped political mindset. And praises fello tribesmen what do does he think he will succeeds from such mindset. He thinks kuyankhula bwino its about god washipping kkkkk and boot licking. The tongue can tell who what he is up to. To hell with your DPP
@fumumdolo7341
17 күн бұрын
Speaker has just expressed brutality no connection to the mentioned kongoresi munthuyundi mwana pa ndale. You are not even a political man. UDF komwe ipite uzizimuka. DPP AND UDF ilipo?
@MecyKamtsuko-me2kr
Күн бұрын
Ngulewakulu
@DanMhone-iw6xg
9 күн бұрын
Mani tangokambani zina ngati zokamba zatha siyani kulankhula koma sitepe mwalowayo palibe chomwe mupezemo boooooooooooooooooon kaliiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiidooooooooooooooo mmmm man timamukonda kwambili
@giftdulamkalenga7344
21 күн бұрын
Mutha kunyoza enawo koma The Dcccc analapa ndipo he is here to stay uyu alowa UDF /Dpp pompa
@YoxyKandawire-kj5vh
21 күн бұрын
Musiyen bon kalindo ndi pulezindet wa anthu osauka ndipo ndiyenkhao akulimba mtima kumenyela nkhondo amalawi
@BillyKalambo-jx3vf
19 күн бұрын
Inuyo mutu suli bwino ineyo sungandiyankhile zopusa iweyo ndalezo unapangapo chani kuchita kuzichemerera za ugalu basi
Пікірлер: 101