imfa ya munthu olungama pamaso pa Yehova pamakhara chimwemwe zilibwino indeed waxy mzimu wa Yehova ukuyankhura iye wangokhara chotengera chake may His soul rest in internal peace 😭😭😭
@ListerMunthali
Күн бұрын
Ndikukumbuka mu ulaliki wina wake bishop kapenga ananena kuti ngati situation ndiyoti sungayisithe no matter what, osalira just say zikomo ambuye. Pachifukwa ichi nane ndikuti zili bwino ndi mzimu wawo for God has relieved him from all his pains🙏
@user-pn7cj9hb3t
Күн бұрын
Chomwe walakwitsa Waxy Kay ndi chani anthu inu? Kapena simudziwa mau simudawelenge?
@WellosMphonde-wd2cx
Күн бұрын
Munthu akamwalira kulira kumatanthauza kusowa chiyembekezo pamene mau ake a Mulengi amati tisalire pakuti mu zonse tidziti zilibwino nde mukati speech yolakwika nde kuti chani. Lolani akulimbika mtima akhale akulimbika mtima pakuti ndi mawu ndipo mwa mawu tidzachuta mwa mawu. Say Amen/Ameen
@user-uo3lm5wl5j
Күн бұрын
Ifa ya wamuthu olungama kumwamba kuli chimwemwe mwAna wazelu kwabassi ndiwochepa agazindikile mawu wayakhula mwanayu Kwa amene amakhululupila mulungu wava tathsuzo lake amen
@MaeCuinhane-gq7ub
Күн бұрын
Ndipo imfa ya munthu oyera mtima imakhala yokoma chifukwa amakhala akudziwa za komwe akupita
@AnthonyChibwe-bf4de
Күн бұрын
He has to say so,, there is no way kut azikhala akudandaula yet zinthunzo zachitika kale komaso sangathe kuzibweza pat. Mmalo moti azingodandaula wasankha kusangalala that's a good choice or adakayankhula zodandaula zidakasintha chan? Umenewo nde umunawo mesa,
@ALINAFEMKOMERA-cm1md
Күн бұрын
He got broken... He wrote a status he was comforted that he should be strong since the father is in a better place Now he is strong anthu muyakhulisaso Mumtima akuliratu munthuyu
@FlorahBanda-fl4vf
2 күн бұрын
Speech iyi ndiyofunika azungu koma ife tiziti mwatilawula😢
@samuelkapasula-mn6es
Күн бұрын
Zoonadi.....Zili bwino mwa Yesu khristu.....
@RedKoffii-gl2vx
2 күн бұрын
Mwana ulimba mtima
@thokozanisukah6448
2 күн бұрын
Indeed zili bwino aliyese azafa komano kuluza munthu sichithu chophweka nde kumankhala makolo ako
@WakisaPhiri-e1e
2 күн бұрын
RIP Pastor 😭 Anthu awa amkavana
@ZaffboyYellows
Күн бұрын
I'm very sorry 😢Your highness young king. If you want to talk ' I'm here at any time
@MalawiSangano
21 сағат бұрын
Mauabwino kwamunthu olungama❤❤
@Choicemlw
Күн бұрын
Yesu analira pa maliro a Lazaro
@user-wz1jy3uj8p
Күн бұрын
❤❤❤❤❤❤
@POker_On1.
Күн бұрын
Zibwíno 🙏🏾
@user-hh4wn4vf9e
2 күн бұрын
Owooo chabwino
@chemapa
15 сағат бұрын
zabodzazo zosamvekazo Mulunguyo anamuuzira kuti? pamaliro sitchukira. tisamaseweretse dzina la Mulungu. kulowetsa chibwana pamaliro a mtumiki wamulungu.
@nkosikhonasiphiwemdlalose227
2 күн бұрын
Some of the tribes in Zim they celebrate when they lose someone zili bwino akapumule ali ndi Yesu wao
@SinyoroMoyo
Күн бұрын
Chitsiru chamwana ,nde chojowera-jowera ndichani .ngati zili bwino osangoyankhula bwino bwino kupereka ulemu kwa anthu ena bwanji.kufuna kutchuka ndi uchitsiru udzazindikira bwino patsogolo
@CatherineKumwendaCatherine
Күн бұрын
Kwa munthu oti amaziwa za kumwamba mwana wayakhura zomwe Mulungu amatilimbikisa pamavuto or pa Mtender tiziti zili bwno
@unarinematshomo2841
Күн бұрын
Muthu akamwarila, timarila pa nthawi imeneyoyo, ndee waxy kay sanalakwitse moti speech yake ili bho ndithu.
Waxy akunena zoona, mau a munthu okhulupilira ndi oti zilibwino. Abale amzanga munthu akamwalira sinthawi yoti ife tizilira ndi nthawi yosangalala chifukwa chani ndikuyankhula choncho, chisanzo munthu akamagwira ntchito kaya ndi pa company kaya m'boma amayembekezera kuti mwezi ukatha akuyenera kukalandira salary, ndiye funso nali, ndindani amene amapita kokalandira salary akulira tipeza kuti palibe wina aliyense amakhala osangalara kuti lero tikadyera nyama, ndi chimozimozi inu ndi ine mulungu anatisankha ndikutisiya pano pa dziko lampasi cholinga chimene anatisiila pa dziko la pansi ndi chani tizimugwadira nthawi ndi nthawi, ndiye tamugwadira mulungu, mwini wake emweyo yemwe timamutumikira uja watiitana tamwalira ndicholinga choti akatipase malipiro pa ntchito yomwe iye anatipasa takhala tikumugwilira tidakali ndi moyo abale amzanga sinthawi yomalira imene ija ayi ndinthawi yotchulusa kupempha kwa mulungu kumupemphelera m'bale wathu kuti ngati anali ochita ntchito zabwino mulungu amuonjezere zabwino zochuluka pa ntchito yomwe iye anali kugwira adakali ndi moyo komanso ngati anali ochita ntchito pena zoipa mulungu asachulukise kuyang'ana zoipa zake Ameen
@kondwanibuleya-br9gr
2 күн бұрын
😢 what a man up
@jamesbowman-cw8ts
Күн бұрын
Koma ndiye Kuli mixed bag of comments,... Waxy this Waxy that,... aMalawi musiyeni mwana, walimba mtima ndi chiyembekezo kuti bambo ake ali malo abwino opumula ndi Yesu wawo ndipo palibe chodandaula,... Ndiye mukuti chani anthu "abwino" komanso osunga "chikhalidwe" chachiMalawi inu?? Pena ngati ndinene kuti dikirani abambo anu akazamwalira muzayankhule speech yanu yabwinoyo,....koma poti imfa si yabwinonso. So whatever, Rest well Bishop Kapenga. We knew as man of God and we're sure to God your soul has returned. Rest Bishop rest🕊️🕊️
Ndalama unadya zacosoma zja nyimbo zake ndizit unaimba?????😩😩😩😩
@jelblinds2017
16 сағат бұрын
There is nothing wrong jst that we as malawians have poor and shallow minds
@MalawiSangano
21 сағат бұрын
Mauabwino kwamunthu olungama❤❤ 0:11
@Tryness-wb6dj
Күн бұрын
Rest well Bishop Kapenga
@patrickjaenda8288
2 күн бұрын
Wavala mzimuwamji mwanau
@user-jn2oc3cn3q
Күн бұрын
Km ine kaya ndi chimodzichi km speech yi sinandivekere mwaumunthu
@AneesaMoosa-nv6bq
2 күн бұрын
Rest in peace bishop kapenga
@JosephJosab
Күн бұрын
Ku show kapena maliro
@LimbikaniChirwa
2 күн бұрын
Sitinazolowele spech ngati izi kuno kwathu
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
Күн бұрын
Mwana wamuna azikhara olimba mtima choncho waxy mbiri yako yabwno umakhara bwno ndi bambo ako ambuye akuze malire amoyo wako ndi abale ako😢
@MalawiSangano
21 сағат бұрын
Mau abwino kwa munthu olungam
@maxyfreeman9691
10 сағат бұрын
Kaya mwanayu sanasute koma
@eltonnankhwere3284
2 күн бұрын
Of course am satisfied with the speech it seems unakonzeka ngati ukupita ku show.i remember you wrote kuti tiyeni mawa tikakumane pa Robins Park ndikaimba nyimbo in other way its not fitting
@ShyreenKwisongole
6 сағат бұрын
Emen
@rabeccadytone8772
Күн бұрын
Wakhutu la uximu wanva
@billykamwendo6517
2 күн бұрын
Ife ndi a Malawi, izi nzachizungu ndipo naaa ine sindingayankhule chonchi ali oti ndi bambo anga.
@TadalaChithope-yg9fo
2 күн бұрын
Azibambo nthawi zambili amakhala olimba mtim and uyuso panja mean oyamba ayenela kukhala strong komas tiyamike kut bambo ake amwalila waxy atatembenuka mtima komas kwaimayife zovuta kom kwa mamun ngt uyu akudziwa chomwe akuchita komas mwa okhulipilila izi zosavuta ngt munawon live yadzulo mayi ake okhala akaz awo anayimba nyimbo xa phamvuso coz ndi anthu okhulupilila and akudziwa kut akuyakhula mulungu wawo
@HussainGaffarOlaiza-hy9sg
Күн бұрын
💔🕊
@DJcliffBandakhudzanga
2 күн бұрын
Waxy ndi nfana olimba mwana wamamuna adzitelo
@mikemakamo7360
Күн бұрын
Koma mwana wakondwelatu 😂😂😂 Zotindipamalilo wayiwala yoh mphamvu ziko likulowa bola
@marryrobert7092
Күн бұрын
A malawi uziwa kurangiza mwana warakwa chani kod simuziwa kuti muthu akafa sibwino kurira mokweza ndemumatu iyi azirira
@FranckieDambah
2 күн бұрын
Eeeeee waxy umatha kuyankhura
@MarthaMfulusa-vj3xe
9 сағат бұрын
Strange
@daziana2023
2 күн бұрын
Zilibwino
@TadalaChithope-yg9fo
2 күн бұрын
😭
@chekiamaabdul5083
Күн бұрын
Muzidyatu bwino ganjayo
@Geraldmkwewu
Күн бұрын
Iyi ndi lmfa osapanga zibwana kawonesa picture yanji kwa azukulu amipingo pamwambo wamaliro kakuti sharp wachani zachamba
@EmmanuelNgamuti
Күн бұрын
Young man where hv u taken the energy to make this non African speech on a day like this?
@DavieChangoima
2 күн бұрын
Sorry rnp
@Ampambachulu
Күн бұрын
Bro thought he killed
@giftdulamkalenga7344
Күн бұрын
Waxy akanakhala ngati chija chinthubidwa cha chilima chija akanag'alura
@MaeCuinhane-gq7ub
Күн бұрын
😂😂😂😂
@SinyoroMoyo
Күн бұрын
Eish guys 😂😂😂😂😂
@robertchitsulo8006
2 күн бұрын
Guys mwanai watani kodi Paribe muthu amasangalala pa ifa ai . Uyu wandikaikisa chabwino R.I.P pastor kapenga
Mmmm waxy Kay Kuno ndi kumalawi ndye yaaa kumbali Ina it's ok kuti zilibwino koma another side this speech is useless to me when you grow up that's when you will realize that l made silly speech RIP Mr kapenga
@user-tb6yh1kx3o
Күн бұрын
Kuyankhula kotani uku, mwana wachibwana
@BlessingsMangwaya-mk4fi
2 күн бұрын
This is not a fitting speech for the day your father passed away 😪😪
@lindamyaba
Күн бұрын
Be serious man, waxy mwaonetsa maturity, zili bwino
@inessmsiyambiri8517
Күн бұрын
Sonotu anthu odziwa mawu zimaaiyana ndi osadziwa mau zili bwino basi ambuye walora
@Melinavituhs-tc8ys
2 күн бұрын
Komatu for sure now irealize rhst crying during someone's daeth is for us poor imagine what is this speech 😭😭😭😭😭💔💔end with sure Anyway rest well pastor kapenga
Пікірлер: 74