Malawi waonongeka basi mmmm mpaka chochi no respect
@JuliousGambatulah-nm8pe
2 ай бұрын
Do you at the end evaluate? The whole convoy is on govt. Allowances, does it do any good for the nation buying cassava for the people, try part B otherwise.......
@CharlesChalimba
2 ай бұрын
But the people are suffering with poverty and hunger
@LysonMkomadzinja
2 ай бұрын
Mw siingatukuke NDITHU aaaa
@FrankHaruni
2 ай бұрын
Kod uyi akupanga sewelo latikufelanji ndemudzuona dzambilidzo ndidzoputsa dzopanda dzer
Kunvetsa chisoni And those people who are following abwelela bwanji kwawoko moreover asiya timageni tawo mma Bench?? Poor Malawi I wish anthu okhudzidwa nonse mutangondilondola kuno ku America kuwasiya anyapala adzipanga manyi awowa 😢
@PepechoGrem
2 ай бұрын
Km umphawi sizinthu ai
@ElizahMadi
2 ай бұрын
Chotsani nsanje Malawi , USI alibe Vuto , kukukumbikila Kuti Moses atamwalila ,Josua anapitiliza ulendo ,sanali Josua yemwe anapha Moses ayi , anderstand about this life plz
@FrankHaruni
2 ай бұрын
Kudula akuine pano 😢😢 pamakepo basi
@hourlyview4226
2 ай бұрын
Zomvetsa chisoni
@jomochirwa
2 ай бұрын
Basitu wosapanga nsanje zosangalatsa anthu aku limbe amulandilatu.kodi inu mumafuna kuti amugende ayi wosatelo .ndikudziwa kuti enanu simudasangalale ndi anthu aku limbe chifukwa chomulandila bwino manganya.
Komadi nde akujijilikatu akuluwa bwanji kodi? Kwinaku ndi kusavukatu. Anaufunadi mpandou etiiiiii
@JamesDaud-jz7uq
2 ай бұрын
Koma zikuchiyikazi kwaona kupusa apolice kumangowayendetsa choncho nkumalimbana ndi gulu la anthu, amalawi amationa kupusa
@AngellahNangoma
2 ай бұрын
Koma jaq kkk
@Moseskapintobanda
2 ай бұрын
Amakwana bwana Michael
@hopemahata687
2 ай бұрын
I feel bored😢
@NelsonMarley-m6p
2 ай бұрын
Dziko laMalawi ndichan I Koma mukuti? Izizi ndizacha? j
@EthelOsman
2 ай бұрын
Zomatithela data za anthu asatanic ayi tikutulukanitu
@MsondaBanda
2 ай бұрын
If you don't have something to say just keep quiet don't shout guys
@NoelKhwimba-bh3ts
2 ай бұрын
Akapitiliza avulala awa akuzimva ufulu ngat iyeyu ndi bakiri muluzi
@CharlesKachipanda-jz9jv
2 ай бұрын
Ndiye zili ndi phindu lanji izi
@alicklongwe5508
2 ай бұрын
Ndinu uwumira nchifukwa mwathawa
@brandinamaloni
2 ай бұрын
Sizikuwankhala ndi ofunika masewelo masi
@EuniceMasambo
2 ай бұрын
Za ziii osangotulutsa ndalama yampamba okwanira asithe business bwa?
@MaxWell-d7o
2 ай бұрын
Athu aku limbe ndinu opepera kwabas
@BlessingsBanda-nh7ur
2 ай бұрын
Uyu nde tikufelanji wenweni😅😅😅😂
@MaxWell-d7o
2 ай бұрын
Takatsitsani feteleza osat mbweleraziyi
@FungulanReuben
2 ай бұрын
Wina andiuze chikuchitika ndichani?
@JoeMackton
2 ай бұрын
Malawi is acting drama for sure
@FrancisMbewe-y1h
2 ай бұрын
Achita bwino a vice president kukawayendela anthu Kuti akaziwonele wokha momwe anthu akuvutikila ndi ma business ang'ono ang'ono poti iwowa safuna kunamizidwa paja zakumva zimapwetekesa mutu
Пікірлер: 132