KZ
item
Негізгі бет
Трендинг
Журнал
Ұнаған бейнелер
Ең жақсы KZitem
Фильм және анимация
Автокөліктер мен көлік құралдары
Музыка
Үй жануарлары мен аңдар
Спорт
Ойындар
Комедия
Ойын-сауық
Тәжірибелік нұсқаулар және стиль
Ғылым және технология
Кіру
Тіркелу
Кіру
Тіркелу
Негізгі бет
Трендинг
Журнал
Ұнаған бейнелер
Ең жақсы KZitem
Фильм және анимация
Автокөліктер мен көлік құралдары
Музыка
Үй жануарлары мен аңдар
Спорт
Ойындар
Комедия
Ойын-сауық
Тәжірибелік нұсқаулар және стиль
Ғылым және технология
Негізгі бет
ALIMI NAWOSO AYANKHULA ZAKU KHOSI
17 күн бұрын
ALIMI NAWOSO AYANKHULA ZAKU KHOSI
Рет қаралды
16,187
HOT 265
1
1
Жүктеу
Пікірлер: 49
@SaidiMbawa-st6bj
15 күн бұрын
A Malawi uchisilu pali zoombera manja pamenepo simukuziwa kuti zithu zambili zaonongeka chifukwa cha kupanga chiganizo mochedwa president ameneyu
@PhillspicJere
15 күн бұрын
Mwabadwa mochedwatu inu kale mwezi ngati Uno chimanga chimakhala chikadali kumunda Ndiye Admarc imagula chimanga chouma kwambiri koma chifukwa chamtundu obadwa mochedwa ndi waulesi chimanga chikukoloredwa chachiwisi
@RobertLuka-wy9cl
15 күн бұрын
Iweyo mchewa wosadulidwa machende ako ndi chakwela wanuyo agalu oyipa
@user-xj7xx2qo3g
15 күн бұрын
Mapazi anu nonse amene mwasokhana kumakambirana zinthu zoti sizichitika mkape wanuyo zingolowa mkutulukira kwinako
@EmercianahKasiku-en6hl
15 күн бұрын
Inu mufuna mulimi wa ku Thyolo ooneka dothidothi zachikale kale ati zigamba zokhazokha ndalama kukapatsa ma Sing"anga
@MavutoNKhoma-pz7qb
15 күн бұрын
President wabwino sitizampeza kumalawi oposa chakwela
@hastingsbnyirongo
15 күн бұрын
Dr Laz Pulezidenti koma ameneyu. Ena sagona Nanu tulo bwana never mind them.
@user-zf9xs3zj9b
14 күн бұрын
Big up Dr chakwela
@user-fi2by2ui9o
14 күн бұрын
Keep it up Mr President develop our Malawi because
@Eric-gb9ms
14 күн бұрын
You mad serious mbamva inu nonse
@CharlesPhiri-ds1rk
15 күн бұрын
Thank u Mr president for your understanding
@alickkachepa3801
15 күн бұрын
I would like someone to tell him kuti Fertilizer wa 4 pin uja apange plan 😢😢😢 notse mli apa ndinu anthu oti sumulima
@yusufsadic2930
15 күн бұрын
Pal mlim panenepop
@MussahIbrahimu
14 күн бұрын
Vuto la asogoleri inu mukuyakhula mokhotesa kumamuuza chilunga president ameneyu wasokoneza kale zinthu mdziko muno😢😢😢
@IssacMateyo
14 күн бұрын
Bwana chimene chikufunikatu sikuti adzimuuza ayi koma kuti inuyo mudziuza athu kwanuko kuti 2025 akavotele amene inuyo mukufuna kuti akawine eetu
@MussahIbrahimu
14 күн бұрын
@@IssacMateyo brother olo abale anga asakhe president amene akufuna ngat a mek atapanga chinyengo ndiye angawine amene ife tikumufuna
@NtchindiChirwa
15 күн бұрын
Alomwe muli mumadzi kuzolowera kupasidwa zisiru za anthu
@CharlesMpaso
13 күн бұрын
Mmalo molamkhula zanzeru iwe wayamba kulankhula za mtundu wa anthu kungooneseratu kuti ndiwe mtumbuka munthu okuda ngati usiku..... Kodi ukati alomwe anazolowera kupasidwa.. Zinthu zomwe akupanga alomwewo akupasidwa ndi boma? Kodi chakwera wakoyo amapereka chiyani? Mulomwe amazilimbikila payekha ukupempha ndi iwe kumeneko coz kuti uwonesese palibe Mulomwe pamenepo....... Ndiganiza wamva mtumbuka iwe okuda ngat usiku.
@user-wi9pe2hz7e
15 күн бұрын
Apindule nd a ndalama kale iz😢
@BwanaGD
15 күн бұрын
Kkkkkk chakwera iwe lazalo uzilembatu sizako zogwira patsayazo kumalemba zomwe alimiwo akudandaula usawatayitse nthawi kulankhula zomwe supanga anyamata Akowo achina unjeniwo akagokubalalitsa bastu uyiwala panja ukugwiraso ntchito mowopa anyamatawo mmmm amavuto amunthu
@danielmsowoya8899
14 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@user-eq8hr8li8h
15 күн бұрын
President opepela ndi. Chakwera
@IssacMateyo
14 күн бұрын
Koma kuti alamule kuti kabichi mudzigula mtengo mwakuti athu muona kuti chakwelayo akusokoneza
@GiftJulius-ro9ev
15 күн бұрын
Palibe chingakumele lwe cadet...panyapako ndi Dpp yakoyo...
@petertaulo8014
14 күн бұрын
Mbuzi
@user-xj7xx2qo3g
15 күн бұрын
Chakwera ngat uli doro kwacha ibwelere mwakali osat zapanozi ndalama yangosanduka manyi enieni
@robertchitsulo8006
15 күн бұрын
Good point no fruits there no agood health thank you
@RaymondKaumba
15 күн бұрын
Anthuwa ali ndi zochita osati cadeti
@yusufsadic2930
15 күн бұрын
Chome chimakhal chodandaulits nchakut mikumano ngat imenei mumaitan anamady bwino okh okh antbu uvutik enienio mumasiy taitanan kt iweyo lazar aitane
@Chiso2019
15 күн бұрын
Amalawi ndi anzeru koma kaya bwnji kayaaaaa
@RaymondKaumba
15 күн бұрын
Cadet kumva kuwawa
@PhillspicJere
15 күн бұрын
Zafika pochitisa manyazi ma cadet chilichose kutukwana?akukupasani bundle yotukwanilayo ndichisiru komaso ndinu mbuli,
@user-uc1pd1tc2x
15 күн бұрын
Ulamuliro olephera zedi Munthu wachabechabe
@user-xd1cm7tm7t
15 күн бұрын
Achewa nokhanokha bas ku start house koma chakwera ndioyipa
@GladsonChikakula
15 күн бұрын
Ķaĝonè
@FastyMakwacha
15 күн бұрын
Iwe zikukusangala mbuzi yamuthu ndi mcp yakoyo tikuonerani
@MustafaLikaomba
15 күн бұрын
Zausilu
@user-uc1pd1tc2x
15 күн бұрын
Mnthakati ya Ya president
@patrickkapinga7091
15 күн бұрын
Ali dyo ngati apangapo kathu koma garu weni weni
@user-uc1pd1tc2x
15 күн бұрын
@@patrickkapinga7091 Ndipo bro, zimaso tudzu Ngati ma robot
@jameskachulu8141
15 күн бұрын
Koma chakwela
@user-oc9vl9xz8e
15 күн бұрын
Im coming to open my farm soon i need loads Mr president keep it up good job
@user-jn9tz3li3v
15 күн бұрын
Waste of time meeting devil wanuyo 👿 mbuliyanuyo siyikumva.
@user-qp8kh2hj9o
15 күн бұрын
Usova cadet wa DPP uwona kuti utani
@FraserNamaona
15 күн бұрын
Ukuyesa ngati nyau nzakoyo awinanso? This country has fucked coz of this guy. He's not presidential material olamulira dziko koma kumpingo basi
@hastingsbnyirongo
15 күн бұрын
@@FraserNamaona usova
@SolomonNjolomole
15 күн бұрын
Anthu opanda chisoni inu oyipa mtima anga mfiti simukuona kuti dziko lanyasa km ma cadets enafe ndi angon central region km zikutinyasa kwambiri
@user-jl6sq3ph1b
15 күн бұрын
Chakwera ndi mbuzi ya munthu siingawineso kae kupepela ichakwerayo amakana kumapeto kuzavomeleza nda achisilu iwowo achakwelawo ka 😅😅
@JailosShadreck
15 күн бұрын
Just west your time
Пікірлер: 49