Bon Kalindo,Kamlepu Kaluwa,Comrade Ntanyiwa,Wanda Msiska and his friend,Brian Banda and others you are really philanthropic and patriotic. May God bless you abundantly.Religious,political, traditional and social leaders here in Malawi are all ordained to the mentality of cupidity hence very unable to transform Malawi philanthropically and patriotically.
@user-fi7ko7bl6f
19 күн бұрын
The DC mwana wayankhulira m Malawi mommuno osati mpakana kukabisala ku Zambia ayi chi Bon Kalindo chinatha mantha ndipo sichiopa Unyolo anta more 🔥🔥 Mr president waife anthu osauka😅😅😅😅
Mr bon kalindo you are number one. More fire Mr dc❤
@priscillamangata4023
19 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣 ngati Malawi ndiwandani Mr DC
@ThompsonMakwakwa
19 күн бұрын
Aaaaaaaaaaaaaa@ koma nde zafikapotu mpaka muchenga machende awo ndithu
@JibuzahDrag
19 күн бұрын
Fire Mr president mumayakhula zilungamo zokha zokha
@user-gm3cx2xn9o
19 күн бұрын
Ife si osauka ndipo sitisilira kukhala ndi president osauka😂😂😂😂😂
@AfricanKingdom-uv1qb
19 күн бұрын
God protect mr DC
@ChristinaSinoyakapawo
19 күн бұрын
Ndabwereza kawili nyimbo yoooo anaphaa mubale wake gwenembe chifwukwa cha udido
@hajrazuwaja4993
19 күн бұрын
😂😂😂amangidwaso uyu ndithu sikusinja ndi gwenembe koma Mr the DC kkkkkkkk
@ChifundoNinje
19 күн бұрын
We love you the DC
@richardkumbambe-tg9qi
19 күн бұрын
Great indeed. Let's all rise ip.
@user-qc5lh3xw2h
19 күн бұрын
Powerful Mr president ❤
@JohnmarkNazombe-hi9xd
19 күн бұрын
Mwana wowopya kwambiri!!!!!!!!!❤❤❤❤❤❤
@user-cg5ml7ym4v
19 күн бұрын
Tili pa mbuyo panu DC ❤❤
@AbdulsEdsan
19 күн бұрын
Mr Kalindo great soldier
@JuuuKomba
19 күн бұрын
😂😂😂😂😂 malawi ndife makape timaopa muthu ot tamuvotela tokha
@ShafieIdrissah
19 күн бұрын
Bon kalindo dddccccc❤
@julietmussa5103
19 күн бұрын
Sikusinja ndi Gwenembe yemweyo....ana amphunzile
@Moses51
19 күн бұрын
The Dc bon kalindo 🎉🎉🎉🎉
@user-ln5hw7dn9g
19 күн бұрын
Ndakhalira kuseka😂😂😂😂😂😂 iweyo ndi wani
@fatsanibanda5213
19 күн бұрын
Yes iweeee ing'alure basi😂😂
@chrisneySwanepoel-yu5vd
19 күн бұрын
God protect mr kalindo
@bamusmajawa1619
19 күн бұрын
Mr Bon Kalindo on fire 🔥🔥💪
@JosephPindani
19 күн бұрын
Km chakwela watopa m'chenga mpaka nd wa boma kkkkkk😅😅😅😅😅
@AubreyBamus
15 күн бұрын
My vote bn
@PeterMoosa
19 күн бұрын
More fire mr winiko
@user-mi3fw1zg8b
19 күн бұрын
😂😂😂😂 Mr DC
@shamimmahomed6709
19 күн бұрын
Bon kalindo yemweyo kuti wawawa!!!
@user-hh4wn4vf9e
19 күн бұрын
😂😂😂 koma ndaseka DC ayi taa sikusinja Kodi
@JuvenileDebwe-bv8ow
19 күн бұрын
kkkk koma chimwana chakwa njedza kkk
@Lazarus-qo1sl
19 күн бұрын
Kkkkkk wapolice samwa ambuye nditengeni
@user-sp4kn8rh2j
19 күн бұрын
Hahaha kwachema 🔥
@user-fi7ko7bl6f
19 күн бұрын
Make mbuuu mwana mbuuuu 😅😅😅
@user-dk6yc8pl2m
19 күн бұрын
The Dc ❤❤❤❤
@thandothando6556
19 күн бұрын
Super super😂😂
@AdiniKhama
19 күн бұрын
Mr DC osafowoka
@Samu-q3z
19 күн бұрын
❤❤❤❤smdc
@user-mx5cx3gl4h
19 күн бұрын
Osafowoka bon kalindo
@user-fd7wj3mg2i
19 күн бұрын
Mulungu azikutetezera nkhondo mukuimenya
@AlexNkhata-c8n
19 күн бұрын
Zoona akunena B kalindo
@user-lr2wx5xd9d
19 күн бұрын
The DC!!!!!!!!!!!!!!!
@user-fi7ko7bl6f
19 күн бұрын
Tang'alulani the DC kuti atongwe-tongwe a MCP amve bwino lomwe. This Boniiii Kalindo the DC, mlowa mmalo mwa Solobala amene ananyongedwa pa makako nda agalu MCP ya Kamuzu ndi John Tembo
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
19 күн бұрын
Bwana apolice atraffic akuonjeza bwerani mnseu wa Bunda every 200m atraffic ndie a area 3 amabwera 3koloko am kuyimba pa mnseu mmmmmmm Malawi
@user-tm6wl5tt3u
17 күн бұрын
Umakwana iweyo
@RabsonSabit-nc5ds
19 күн бұрын
Uyu ndi nyoooo
@JasperKaleni-dx6nn
19 күн бұрын
😂😂the dc
@WITTNESSMBOBADINHONJOLOM-bv4un
18 күн бұрын
Bon kalindo tili limodzi
@PachaloShaba-pf5vw
19 күн бұрын
Good boy
@van-wykchilapondwa6981
19 күн бұрын
Great 👍
@TiyanjaneMkwate-we8gu
19 күн бұрын
Kkkkkkkkk koma a Kalindo agogo anu ankakuuzani nthano ya sikusinja mukupita ku nzuzu , ndiye mwati ankakuwerengeranu mu chikangawa? Komanso mwati anaphana chifukwa cha udindo? Ndipaseni page ndiwerenge nawo basi . U are number 1
@WisdomMaseko-fi5sv
19 күн бұрын
Avu
@WisdomMaseko-fi5sv
19 күн бұрын
Lyton Mangochi bwerani yamanja ija kuno
@MemoryKamanga-jv4jh
19 күн бұрын
You are welcome Mr dc
@irenioeugeniosumila6647
19 күн бұрын
Ulemu wano A Kalendo
@frankdonovanntambira
19 күн бұрын
Ndipo Boma Lamanyi ngati ili ine sindinalionepo Aaash!!
@IssahAluba
19 күн бұрын
aaaaa zayambika liti tchega omwewu gati mwatopa nawo phandowo apatseni ena MCP is very nonsense iyaaa
@griviniakanjaula4456
19 күн бұрын
More fire mbuyanga alomwe alomwe nophiya
@user-ng4ic8jo8b
19 күн бұрын
Koma iwe ndigalu kwambili
@RichmanNkhoma
19 күн бұрын
Mbambande me. Kalindo
@user-vq6zr4tn8v
19 күн бұрын
Muma tiimila osatopa
@SaidiMbawa-st6bj
19 күн бұрын
A opposition zochita zamwo ndi zimodzimodzi
@JohnZyambo-q8h
19 күн бұрын
❤❤
@user-pv9uk6sc3w
19 күн бұрын
Kulephera kuja ndi kumeneku, anthu ndi okwiya kale , atopa ndi boma ili
@Chipilirodaniel1989
19 күн бұрын
❤
@scoltenroma6240
19 күн бұрын
Kuswa kuswa😂😂 akavote ndiamawo Oh yes 🔥🔥
@JohnZyambo-q8h
19 күн бұрын
🎉
@JeanBanda-zy6wu
19 күн бұрын
Koma ndiye mwafikapo mpaka kulesa anthu kuti asamavuule mchenga really? Nyumba zanuzo munamangila mchenga munakawoda ku America? Silly people
@SarahMusama-eu7wt
19 күн бұрын
Atsala atigulitsa mphweyaa kwatsala
@TapiwaKhwisula
19 күн бұрын
Mo faya mr dc
@SilenceChepiano
19 күн бұрын
DC ndimava kukoma mukatiyimilira
@charitykalua8507
19 күн бұрын
The DC😂
@JamilahChitulu
19 күн бұрын
😂😂❤
@Aisha-db6ds
19 күн бұрын
Eeeee koma ationjezadi apa ndiye yalakwa,, Tipindilana ndenvu mkamwa ulendo wake ndi umeneu
@MecyMalothi
19 күн бұрын
The D C!!!!
@GanieAlidih-gu7no
19 күн бұрын
Anapha zake chifukwa chaudindo
@stevejizaremu3396
19 күн бұрын
The DC
@StanleyChirwa-d6b
19 күн бұрын
Koma Chaka chamawa tikhapana ndithu
@oskidooscar7468
19 күн бұрын
Koma why sakuyamkhulapo za manganya ku mcp palibe audio olo imoz inakambapo za Mr usi
@EmmanuelGasiten-fo5dr
19 күн бұрын
Ipondeni Fadah
@SolomonShaibuh
19 күн бұрын
Ndkhulupilira kut a Malawi mistake iyiyi sitizachitanso
@FrancisChimwaza-t7d
19 күн бұрын
Iswani ndithu man wamkulu ndi mulungu basi
@phillgatoma4857
19 күн бұрын
😢😢😢😢😢😢
@KennethMchenga-j9c
19 күн бұрын
Pliz a DPP tadzukani kodi mukunafuna amalawi atani
@dalitson3558
19 күн бұрын
Ndipo zomwe akupanga a Dpp akumabowa kwambiri anthu akuzunzika ndi boma Koma aliphee ngati akumetedwa
IWEYO ndi opusa kwambiri ndi chakwera wakoyo ngati akutuma cadet mbuzi, ngati iwe ukidya ndi mcp usawanyase AMALAWI AKUVUTIKA , ndiye uzikayankhula mbwerera zako zankutuzo , ngati sizikusangalatsa amakutuma kuti uzimvera ndi ndani ulibe manyazi ? Cadet supit
@isaacchiwaula731
19 күн бұрын
@@HalisonSolomon ukufuna ndikuyankhe? Born kalindo umamudziwa? Zomwe akumayankhula amayankhulira iweyo, it's wat u think? Ok kavotere amene ukumufunayo n uzandiuze kut zinthu tsopano zilibwino pamoyo wako. Kalindo sankatukwana DPP ndi Peter munthalika? Lero mwaiwala
@StanleyChirwa-d6b
19 күн бұрын
@@isaacchiwaula731 inu musokosa mungosiya kuverako bas sizokakamiza izi boss
@HalisonSolomon
19 күн бұрын
@@isaacchiwaula731 iwe sungamakhale KUMBUYO kwa mcp ngati sukuona momwe dziko lavundira ndiye kuduka mutu kumeneko , usiyamitse mene chakwera amatenga boma linali motani ndiye pano zilimotani ? Ndiye timusiye chakera alamuleso lidzakhala dziko? Anthu adzakhala ngati ndani, tiyeni tiganizire ana omwe taberekawa tisakhale ngati a police ndi asilikali amene asankha kigwira ntchito ndi chipano malo moteteza malamulo adziko,
@BudaEarth
18 күн бұрын
U na problematic
@chadreckchibwithala1493
19 күн бұрын
DC PANTCHITO IFE WOZIWA ZINTHU WE KNOW KUTI ABONI KALINDO ALIPO PA NTCHITO YOSUTSA CHILICHOTSE NDE MUWONE ALOMWE AVEKERE EEE OOOO UUUU KUKUWA AGALU ACHILOMWE MKUNYA MCP IS GOING NO WAY 2030 WOOOOO CHAKWERA.
@JeanKambala-gm1zr
19 күн бұрын
Zosantheka Brazil ndipo idzankhala yazikwanje zomwe² mwaphela saulosinever again MCP achimwene
Пікірлер: 117