Ngat ife amalawi tilibe mawu action pa 10 July bs the dc Mwana oopse kwambili❤
@marthablessings1314
Күн бұрын
Bwana waanthu osauka..we dilute u🎉🎉🎉🎉🎉
@chekiamaabdul5083
2 күн бұрын
Your sense mr kalindo is very powerful like the Kenyans people they don't tolerate nonsense . it's only you the all fucken Malawians you deserve brave enough i like it.
Kkk nsapato yonyamuka ku tsogolo ngati kukamwa kwa nsomba i ❤️ you Bon K umanena chilungamo
@user-wx7pw8xg6x
2 күн бұрын
Ulemu wako DC umakwana
@FrankPhiri-f9w
2 күн бұрын
Very Very good Bon Kalindo
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
2 күн бұрын
Bwana Kalindo mukunena zoona ndipo Boma ili mmmmmmm apolice tili pamavuto bwana ndipo ma uniform omwe akuvalidwa panopa ndi anthawi ya Bingu ndi peter mutharika zomvesa chisoni Bwana, ndikungoona kuchedwa 2025 Chakwera is a destroyer
@GanizaniKamvazaana
2 күн бұрын
Ndipo Malawi amene a kusangalala ndiomwewo saname dziko lathu ayi saname tithera moyenda momwemu koma na kumalawi adzapita chakwera achoka ndipo eeeeish 😢
@user-ez1kc7zp9m
2 күн бұрын
Chakwera,s brain is divided into two parts.1part is full Of evil & the other part is empty
@sarahmphande6108
Күн бұрын
Zipalasilo za nkhuku abale koma Ali ndimaphunzilo awo shame
@HopesonJailosi-vd6ou
2 күн бұрын
Ku South Africa or zimbwete zikupezeka,anthu akuzuzika
@BrinoMvula
2 күн бұрын
Mmmmmm mpaka transfer kumaiko ena
@ShafieIdrissah
2 күн бұрын
DC ❤❤❤❤exactly kale police imaopya komalele aaaa manyaka😂
Пікірлер: 97