Yooo broh koma munafasatu mchimwene apapa km ndaseka
@EsnartGirivin
Күн бұрын
@@RaffickAllie 🤣🤣
@robertzambia8697
12 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@merryMaele
Күн бұрын
Kaliati anonetsa chikondi kwa SKC ku makhoti kuja amakhala naye pambuyo mmavuto muntendere anali naye SKC.
@StandBwanali
Күн бұрын
Mai Kaliyati, mpando mutenga uwu
@FracksonMadani
2 сағат бұрын
Enanu mpatseni support Kaliat, ngati simukufuna kumthandiza, tulukani mchipanimo😂😂😂😂Kaliat my vt
@JohnFrank-cg1yh
Күн бұрын
Mayi kaliyati my vote, chifuka manganya si wa utm skc anangomutola penapake, ndichifukwa salemekeza mzimu wa skc akanakhala wa utm weniweni akanamuuza chakwera kut imfa ya chilima ifufuzidwe
@RachelMbvundula
Күн бұрын
Mayi Kaliat mtima wawo wonse ndi UTM amayikonda koma agwirizane onsewo
@Andrew-nz9sh
2 күн бұрын
Kaliyat my vote
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
Күн бұрын
Mai kaliati my vote to be utm leader
@DavidPhiri-o6w
Күн бұрын
Kamba koti Malawi kuganiza kochepa , mwini chipani anasankha kale ndi Usi... Chilima was not stupid kusankha usi the whole Malawi
@ebenezerkamanga6016
2 күн бұрын
Kaliat is fitting right on that position
@RoseThindwa
2 күн бұрын
Mai kaliat
@NoahMunthali-m8x
Күн бұрын
Kaliati ndi 1,akudziwa komwe kwachokera chipanichi
@AubreyWilson-j8w
Күн бұрын
Vote for mayi kariyati enawa angofuna kuolokerapo ndikupha chipani koma mayi uyuyu in no matter what ❤❤❤❤
@DalitsoChikanda-r1d
Күн бұрын
Kabambe is a best teacher
@MakabaBauleni-c2i
Күн бұрын
Akweni akuenera kutenga mpando acoka kutali ndi skc
@LingsoneChitsulo
Күн бұрын
My Vote - KALIATI. 1. Ali ndi experience yokwanila kukhala president wa chipani cha UTM ngakhalenso dziko la Malawi coz wakhalapo mma unduna osiyanasiyani mmaboma angapo apitawa. 2. Wachisunga bwino chipanchi mu mnthawi yozwizwitsa yomwe chipanichi chadutsamo ndipo wathandiza kwambiri kusunga legacy ya UTM on behalf of the late SKC. 3. BUT, should work together with the rest 3 excluding the vp. 4, If this party will going into power in 2025, Kabambe should be appointed minister of finance.............my opinion.
@TamikaKaponya
Күн бұрын
Kaliati is the best...azibambo wo tu kuwina akukapanga alliance ndalama analandira kale
@isaihmagani5697
Күн бұрын
Zoonaditu
@emmanuelhassan-v1s
2 күн бұрын
Kaliati
@lindagombwamakuta5828
Күн бұрын
Kabambe my vote . He is an economist.
@TressLuka
Күн бұрын
Kaliyati emweyooo
@AbrahamLLoyd-xb2xc
Күн бұрын
Kaliyati vote
@doreenkaliati3166
Күн бұрын
Mai Inuyo aaaa Palibenso mmalawi muno Ife misonzi yathu ikuyang'ana pa Inu musatitaye chonde ndife ana anu Mai Kaliati chonde chonse tikaona inu ife si amasiyenso ai kukulilirani Tikaona inu Taona Chilima Maiko usi achokeretu ndithu ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@susantembo2076
Күн бұрын
Mrs Kaliati has the vim vigour and vitality to lead the party and the nation. Her plans for the county’s economy will help the country to grow.
Kuno ku Mozambique tikufuna malawi itatsogoleredwa ndi mai kaliyati.
@geoffreykankhomba
Күн бұрын
I hope tavota kale APA kaliati president and ku conversation tikasankha maudindo enawo hon kaliati kulowa opanda kupikisana ndi munthu wina mukuona bwanji
@isaihmagani5697
Күн бұрын
Nkhani ndi Mayi Kaliati basi azibambo enawo ndi oti azagulitsa chipani ku Alliance ndi zipani zina,pomwe Kaliati ndi mwala mwala machine wachoka nayo patali UTM
@EdenNgulube
Күн бұрын
Mayi kaliyati munthu wanzelu kwambili pamtendele komaso pamavuto tilirimodzi this can be my vote
@OmegaChingamuka
Күн бұрын
Mai kaliati more fire 🔥🔥🔥💪💪💪🔥🔥
@MosesChazima
Күн бұрын
Akweni imwewo❤
@louisbonongwe8537
22 сағат бұрын
Kaliat ndye oyenera... Enawa anali kut nthawi yonseyi? Kaliat was with skc in bad n good times and akuziwa zambiri za skc than ena onsewo including usi himself
@SteveSteveJumah
2 күн бұрын
Kaliat for sure 🎉
@FredMpawa
Күн бұрын
Akweni omwewo basi ndinthu ❤
@SamuelJoseGaviteni
Күн бұрын
Amai omweo
@ToweraGama
Күн бұрын
Knowlege is power, kanambe
@DoreenMuhota
Күн бұрын
Kaliati❤❤
@amonechirwa
Күн бұрын
Dr kaliati 100%
@LoleniShabani-mt7nz
Күн бұрын
Kaliyati is not a coward
@BlessingsmadalitsoShumba
Күн бұрын
Mai uyu wanyamula mzimu wa SKC ndipo atha kusintha dziko uyu akusiyana ndi Mr chikangawa wakupha naiwala njala mziko PATRICIA KALIATI VOTE 🗳
@HamzyRashidPhiri
Күн бұрын
Za one million job usatinamize iwe newton ife amalawi si ana ako iyayi wava mapwala ako
@FisherAction
2 күн бұрын
Kaliyt bola
@AnnieJumaNaitanda-qj1iz
Күн бұрын
Doctor P K Akweni
@orpamalunga6925
Күн бұрын
Mtumbuka vice Kabambe
@PhillipJosephy
Күн бұрын
Ok
@susantembo2076
Күн бұрын
Dr Kaliati
@0wenNkhambule
Күн бұрын
Kabambe number one ❤
@AdamuKasimu-x5o
Күн бұрын
Usi achoke apa tikumufuna kaliyati
@BrooklynYayo
Күн бұрын
KABAMBE...... KALIATI WAYAMBA KUNDIDABWIXA....AMULEXA BWANJI KABAMBE KULEMBA KALATA KWA USSI????
@wezienyirenda
Күн бұрын
Kaliati,Kabambe and DPP same Watts up group.If one these two wins I see DPP team B.
@InessMchenga
Күн бұрын
Akweni my vote
@GeraldMkwewu-gd5eb
Күн бұрын
Walimba nazo mama kaliati osati enawo achina kabembe akubwera atawona poti chilima wamwalira angwire naye ntchito mayi walimba nazi uyu
@MariamAli-k5j
Күн бұрын
Akaliayat nde utm yooooo
@wezzieneba9238
2 күн бұрын
Azibambowa angora a mpando basi. Mayi Kaliyati ca do better.
@AmisiDytoni
2 күн бұрын
Kaliyat
@UnicekapachikaHanzwell-zz8te
Күн бұрын
My vote kariat
@DjshukulanGift
Күн бұрын
Kaliyat basi ndi emwe Anali pamavuto even patendere ndi chilima,osat sukusija usi
@JohnBanda-ux9fy
2 күн бұрын
Kaliati Munthu oganiza bho
@Malawian-q5f
2 күн бұрын
Dr kabambe
@Costance-nf7ue
2 күн бұрын
Kaliati weniweni wa shooo
@cmsanyama200
Күн бұрын
Ndaganiza bwino my first choice is Mayi Kaliyati and I have no second choice.
Пікірлер: 274