Wow I lavuzi you Che Mandota,inu ndi dolo basi💪 Lesson learnt,more love and respect for you from Lusaka Zambia 🇿🇲
@user-tk6qh9zs7h
9 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 Che Mandota inuyo ndi number one. Ili ndi phunziro labwino kwambiri osamangolandira ziri zonse musanafufuze za zolinga zake. Keep it up Che Mandota ❤
Phuma ndi ndalama che Mandota😂😂😅iiih ndafa ndi phwete...keep up the good work😊
@user-lh9ue5np8o
9 ай бұрын
😢😢sikuti siku lithe uyu asanapepere ayi ndithu,as a Matala of fact
@Jared57H
9 ай бұрын
Ndota APA nde ukala opanda siwalotu😂😂
@sharmarclongweh
9 ай бұрын
eeeehhh koma iyi katundu wapha😃😃😃🔥🔥🔥
@user-fh5yn8xk2k
9 ай бұрын
Koma iwe wakulila kumangamba❤❤❤❤😂😂😂
@jefreykazembe8691
9 ай бұрын
Muli uthenga wa bwino kwabasi.... Umakwana chemandota😂😂😂🙏🙏🙏🙏
@Wesleywisk-lf5hw
9 ай бұрын
Chemandota kukonda ndalama ndye ndizimenezotu 🤣🤣🤣
@espee18
9 ай бұрын
Koma ndanseka 😂😂 mandota iweyo ndi galu kwabasi
@user-yw3co9yt5y
9 ай бұрын
There's a good lesson for those who are interested in looking for benefits while ignoring the effects
@Fatima-ck3mu
9 ай бұрын
Akadule basi 😂😂😅mandota wasala dzina lokha
@lukemanda1451
9 ай бұрын
Mologeni adzakupweteketsani 😂😂😂
@futuremoyo5714
9 ай бұрын
Tiwona zina zache kuzogolo ku😅
@ushershamighuna1228
9 ай бұрын
Mene tilili kudikira 😂😂😂😂😂
@takkomacomedy1566
9 ай бұрын
Mundu wamkulu mwandizangalaza kulimba mtima 😂😂😂😂😊
@MaimunaGolden-nj3vp
9 ай бұрын
Kumafunsa kaye a Mandota🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@ChiefJustin-cl8jl
9 ай бұрын
Sipatsalapo kanthu Ata 😂😂😂
@christophermsowoya741
9 ай бұрын
We've been waiting timaona kuchedwa
@user-qd6rd5kg3p
9 ай бұрын
😂😂Mduleni ameney
@user-oc2nj6ld4i
9 ай бұрын
Chemandota kumafusa kaye 😂😂😂😂
@AbdulraheemWilliam
9 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂 upongwe waiting next part ,but am worriying that ur ambassadorship with Inno build its over but i wish u all the best till u find another one still u support here from SALIMA Town
@user-ei8dn9my9d
9 ай бұрын
Nyambalo kukaiotcha😂😂😂😂
@Blavk-ic3
9 ай бұрын
Usadzamwalire ase. we lafvs yu tu mach again😅😂😂
@alexbanda8463
9 ай бұрын
Center yapita 😂😂you😂
@ibrahimwilless3414
9 ай бұрын
Ache mandota kumafunsa kaye mmmm apa nde Akita wafa 🤣😁😁😁
@user-no7ib2fs2d
9 ай бұрын
😂😂😂 are mandota uxandipha ndi kusekha kkkkkkkk
@josephchibisa6423
9 ай бұрын
Mandonda kukonda ndlama wakumana nazo😂😂😂😂😂😂
@user-go5bx9gg1v
5 ай бұрын
Chemandota changu mpaka kudumphila nzere 😂
@user-ym6xu3xt2i
9 ай бұрын
Inu a chemandota kulandira ndalama osafunsa kuti ndizachiyani mudzathetsa ana samalani.
@user-jn5er5zu2f
9 ай бұрын
Kupupuluma akulu, nde akukakuchosanitu😂😂😂😂😂
@Loytee463
9 ай бұрын
Akita opanda ziwalo 😂😂😂😂
@user-lh3ib8qm9z
9 ай бұрын
Koma mandota phuma kkkkkkk aakuti chigoba chachimanga mukuchidziwa😂😂😂😂😂
@KupeSuwed-db5cr
9 ай бұрын
Koma mandota panka kulowerela ndilama zaena kkkkkkk I love you
@anniewhite3497
9 ай бұрын
Nthawi zonse umafa mandota😂
@patiencemkonde1145
9 ай бұрын
😂😂😂 mandota sazatheka
@stankaphinde7259
9 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣 always hillarious. I like the ending
@clementpprotazio4781
9 ай бұрын
u don't want peace you want problems always mumatha Inu I loves you indeed😂😂
@fefa2050
9 ай бұрын
Mandota I'm warning you tsiku lina suzasala mkathu sure coz ukuoneka kut ndalama umazikonda heavy kkkkkkkkk
@ChisomoChidothe-fv7yf
5 ай бұрын
Koma aise Mandota dzuwali munthu kjmagogawa ndalama za ulere umaganiza bwanj?😂😂😂😂😂😂😂😂😂 eeee ndaseka and is good lesson to us.
@MosesMvula-te2nf
9 ай бұрын
😂😂😂😂 aaa iwe nd dolo aseee.
@freedauswaison9077
6 ай бұрын
Iweyo. Umakwannila ❤ayilafiyu tumachi
@LindaChithumba
Ай бұрын
Kkkkkk ndaseka kwambil mpaka kutsamwa.kkkkk kumangolandil ndalam osadzwa it zikuchok kt kkkkkk k km mandota
@kennethmajor-zm4pt
9 ай бұрын
Koma mandota uzathera mmanja🤣🤣🤣
@corneliusphiri5519
9 ай бұрын
😂😂😂😂Koma Ka Dokotala akaka
@emmanuelnambazo8212
9 ай бұрын
Akulu inu kugundika uku Mayili asatengere😂😂
@apatsakalonga7740
9 ай бұрын
Haha uyo apa nde Akita wafadi basi wagulitsa centre 😂😂😂
@alickmajiya
9 ай бұрын
Mandota suzatheka kkkkkk
@james2002walita-wc4tr
9 ай бұрын
Mandota puma kumafusa kaye mmm m😂😂😂😂😂
@promisemakawa1556
9 ай бұрын
Chemandota, safunsa anadya phula😂😂😂
@user-fn7eh4hd7x
9 ай бұрын
Umakwana ❤❤❤
@rajabinussah6107
9 ай бұрын
Kumafunsa pa malo ukafika mdyomba 😅😅😅😅
@iconictkn
9 ай бұрын
First to watch and comment 😂🔥🔥
@Muslimvoicemalawi
9 ай бұрын
Koma kumeneko 😂😂😂 che Mendota iweyo 🤣🤣🤣🤣 usazafe uzangosowa
Пікірлер: 322