Ndiwokoma mtima atithandiza father wathuyu akhala bwino
@margetjustin7170
3 күн бұрын
Ambuye apitilize kukupasani moyo wathanzi
@amonbanda6977
2 күн бұрын
Good suggestion...
@CyprianoSandalamu
3 күн бұрын
Koma ndimati tipepheko ,Kodi sizingatheke kutenga account number ya sir Paul Banda kuti mwina anthu ambiri tilikutali mwina kungatheke kumatumiza kangachepe through bank account.
@amonbanda6977
2 күн бұрын
Number it's there pa screen check properly boss....
Пікірлер: 16