@@gomezthera535 Okay iweyo uli ndikanthu boss than him, thanks.🙏🏿
@RichardRomoliwa
8 сағат бұрын
Akudalitseni Yehovah musalekere pomwepo. Athandizeni ndi zipangizo za ulimi
@CharlesjeremiahNyirenda
3 сағат бұрын
Nyemba yako Joyce banda mrs chikangawa .. Atumidwa ndi manyi a chakwela panya pako and Rip.
@LeyvanSamuel-pe5tc
21 сағат бұрын
Keep it up good work 😇 mayi WA fuko
@DONNEXKhama-bk1gy
Сағат бұрын
Thanks alot
@IigIgf
22 сағат бұрын
Well done amayi ❤❤❤
@ThomasJohn-qt2jn
9 сағат бұрын
Ulemu wanu mama😊
@MillieMalakam
22 сағат бұрын
Wallah pule athu ndi wopepela kwambili Inu feteleza akukanika misewu ai kulemba anyamata ntchito ai koma chimeneco akuziwa kuba ndalama kumagayila athu ma2pin zazii
Ngati ku under 5 abale mmmmm zinazi kma eeeee... changu akakupe phala eeeee
@mollymasangano473
22 сағат бұрын
Ha Anthutu ali ndi njala.while President of Republic of Malawi ali busy ma Push up pa Seu wa BLANTYRE Pa BLANTYRE Majesty around about pola pola ma Push up while my Fellow Malawians they don't have FOOD tawonani anthu Wonsewo alibe chakudya komanso Chimangacho Chachepatu ,SAD.😢
@MillieMalakam
22 сағат бұрын
February athu awa simungawone akugawa chimanga koma thawi ino yakapeni ii amawoneka ngati athu abwino zazii moti. Chimanga agule chambili akasiye mwadimac muthu winaaliyese azikagula ekha agawa nkangati
@ROSEKATHYOLA
22 сағат бұрын
Mayi Joice Banda ine ndikupempha mundilembe ntchito zoasidwazi aizindikwanula Koma ndikufuna nzikugwilirani ntchito inu muzindiasa ndalama
@PhalesNotta
22 сағат бұрын
Ndipo inu anthutu aphana chimangachodi ndiy chachepa komabe choncho agawana pang,ono pang ono anthuwo ndiy achulukadi zoona bas mulungu ndiwabwino
@FatimaKananji-kz6yx
18 сағат бұрын
Maindimai basi Allah azi onjezela malisk mwachosapo mulungu sa odika pakomo kupasa muntu zosowazake km zimanstela mwamuntu osasiya ntima unenewo asalipila Allah Allah sachedwa sa fulumula pempelo langa Allah osionjelela mwachosapo mawa mugawile zo ena stiku lopambaba
@DesmondTaulaye
3 сағат бұрын
Chikangawa achite manyazi
@AbuduRajjabu
19 сағат бұрын
Koma sogoleli amenewo til naye panoyu ndiwozikonda kwambili inde kuthandiza sikolesedw koma bwezi akuyamba aboma enawa ndikumabwela pambuyo koma ali duuuuu
Responsibility ya boma kupanga izi coz achakwera akungoyenda kuononga ndalama za boma ndi nduna zake anthu akufa ndi njala APM agawa chakudya nthawi yake ifika .
akuyesesa kumbali yake mayiwo kwinako enawo apite chikangawa
@ChimwemweSauka
21 сағат бұрын
Ndi wa MCP uyu asatiputsitse
@JamesLongwe-qz9fd
21 сағат бұрын
Mayi chaka chino pangani za nzeru musapangeso zophatikizana ndi mcp
@LeyvanSamuel-pe5tc
21 сағат бұрын
Olo akugawa nyumba ndi nyumba sangawine paokha amayiwa ngat anaberedwa aliboma
@JohnesGama-cz7ph
22 сағат бұрын
Koma nzoona izi ,kuno ku Malawi zafika APA?
@MarkKumpoto
21 сағат бұрын
Mavuto anu amayi awa ,paja munapakula zambili kale ,sitinaiwalile
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
22 сағат бұрын
Mayi uku nde kukhala.chakwera akukasewera golf anthu akufa ndi njala.
@marthaphiri3600
2 сағат бұрын
This is due to bad leadership qualities. Anthu ankuvutika conchi Moti ma polotishani akumadyelela m'manyumba mwao, zacisonitu izizi!
@chippakaribafox2865
4 сағат бұрын
Mbava iyi....she must payback to the community.....she started all this problems by accepting tricky move from imf to drop kwacha currency so that malawi can continue to bow.....very stupid woman
@MaryTchapo-py4hh
22 сағат бұрын
Azimai anapepera mwasanga kukasakha molakwika
@GiftJulius-gx2kb
20 сағат бұрын
Mukatele chikabwela chisilu chama baki chija muzichiombela mmanja
@MCAnthonyNdau
19 сағат бұрын
Iwenso ndiwe chitsilu ndi mbuyako emweyo
@GiftJulius-gx2kb
20 сағат бұрын
Mayi uyu kupeleka ndiye amatha
@RoseThindwa
21 сағат бұрын
Bravo
@Paworo-h5r
21 сағат бұрын
Muzimayi ambuye akudalitse
@RuthChilobwe
21 сағат бұрын
God forgive your past sins madam.joyce Banda
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
22 сағат бұрын
Mankhwala akugulisidwa ndi madoko omwewo.
@cictechnologies1091
21 сағат бұрын
Akuwomba m,manja mwamphavutu
@CadTafa2
16 сағат бұрын
Sizingatha sisani fetileza
@VitumbikoKaunga
23 сағат бұрын
Kuja anthu amadya chiteze komano
@MarthaMbewe-uk5nn
23 сағат бұрын
KOMA CHIMANGA CHO CHIKWANA ANTHU ONSEWO?? ZOSAYENDA
Bola mbale ziwili akagayise adyeko pang'ono kusiyana ndi chabe
@StevenKapalamula
22 сағат бұрын
Kwandani ukuku
@SaidiMbawa-st6bj
21 сағат бұрын
Peter wamuthalika ali mbali ya komweko koma zosamukhuza ayi Chakwela ma vote ake Sali kumeneko opposition yongona
@RiteRoderick
20 сағат бұрын
Ndiiwe garu zedi, opposition yogona Joyce Banda si opposition???? Munya muona mukhaula DPP ikunvesanibe pain simunati Peter Munthalika ndi Boma amwene 😂😂😂😂😂😂
Пікірлер: 103