Mmmmm...inu Gagayo moti Anthu azidya ndi Njala yake imenei....mbwanji osawauza kuti azikumba Zimbuzi zomwe zinazaza ndi Manyi...!!!...n'kuphatikiza ndi Ndowe zambuzi.
@PatrickSomanje
2 ай бұрын
Tikuwafunabe mr muthalika ife
@PatrickSomanje
2 ай бұрын
Akuwawopa a president a Dpp is a gd leader for malawi
@AliAli.aliheassim
Жыл бұрын
Nkhanga zoona morefire
@AbudulahMalango
3 ай бұрын
Ine niliwokodwa. Kwambiri pazimene mumalengeza leloamalawi tapenya chifukwa cha thanyiwa
@FionaKhoma
Ай бұрын
Kod report landege lichoka bwanji ku German pomwe chakwera analikonko kukawapatsa ndrama kukupusitsan ngt akukakwera njinga pomwe amasiya ndrama kut apereke report labodza
@leonardjika2100
11 ай бұрын
THAT'S NONSENSE TO TALK ABOUT MIKOZU FROM PEOPLE THAT'S STUPID GARBAGE EVIL IF IT WAS FOR GOATS AND SHEEP WAS BETTER DON'T TELL US USELESS EVIL METHODS
Пікірлер: 29