I started following your prophecies in 2013 when you prophecyzed about the VP, APM, AM and LC
@omanm2919
6 күн бұрын
Thanks prophet for your massage and open us
@LumbaniNeba-d9n
7 күн бұрын
Thanks a prophet for great and message yotichenjeza
@GraceLimani-zw7dx
5 күн бұрын
Amen man of God u re really prophet of God ndayamba kukutsatani zonse mulungu a ayankhulane zakwanilitsa mulungu pitilizani kunenela a kugwira ntchito mwa inu
@symonmpira9403
6 күн бұрын
First time to see this prophet , but looks like is very powerful indeed ,lemme start following him now
@GoodmanNzunda
6 күн бұрын
God will not do anything without revealing in his prophets may God continue to use you man of God
@user-ey5wx1eu5y
7 күн бұрын
God has spoken Let us honour Him❤❤❤
@EstherJamesChipembere
6 сағат бұрын
Ambuye atichitire chifundo ndi kutithangatira kuti mdziko mwathu muno mukhale mtendere ndipo tichite kufuna kwa yehova
@user-nt8po2sk8x
6 күн бұрын
When God's servant speak forth the wise listen
@TwalikiWisiki
4 күн бұрын
Man of God I agree with you, God told me that the president of this country has two choices 1.public confession regarding his hands involvement the death of his VP,, 2.or keep on being stubborn kill many so as to silence people from talking about this ,arrest many to instill fear in them so they don't cry, talk about, But what ever he does God's wrath,, is on him and his children, Gic said he is going to expose him like it or not just like he did with king David when he killed his soldier and took his wife,,God said it's high time he is going to expose him for using His name to do Evil,,He said this man will know no peace,, aMalawi tilape chifukwa cho limbana ndi mtsogoleri amene Mulungu adamusankha,,nkuyikapo munthu yemwe Iwo a Malawi amamufuna,,that's where the nation went wrong,,
@ChanceMax-kw9wf
5 күн бұрын
True sir Lucius is no more😢
@ImranShaibu-ir7gv
7 күн бұрын
I can see it in his eyes that the prophet really had deep love for the Departed vc
@user-mo5od8cy3n
3 күн бұрын
Ngati salapa ndi kuyankhula pa chilungamo pamanso pa dziko asiyeni osawakakamiza
@TwalikiWisiki
4 күн бұрын
Oti alape ndi iyeyo,, ife sitinaphe nawo a Chilima ndi anthu ena 10, honestly speaking sindingapite Ku ma pemphero amtundu wina ulionse ndi a MCP never,,
@EstherJamesChipembere
6 сағат бұрын
Tigaoreni number yanu a prophet
@AlufeyoBanda-cv2we
7 күн бұрын
Ndimangodabwa kut kod dziko lapasi chimachitika ndichani ma prophet abodza amatchuka kuposa ma prophet enieni ,ndipo amakhala ndi mafollowers owapanga defend
@clementmahoka6287
5 күн бұрын
kkkkkkk
@isaihmagani5697
4 күн бұрын
Zoonadi ma Prophet ambiri abodza ndamene Ali ndi anthu ambiri owapanga Deffend owasatira ndi ambiri poti amadya limodzi
@yassinn5634
2 күн бұрын
@@isaihmagani5697Pajatu osaiwala bodza ndilokoma kuposa chilungamo ndi chifukwa chake anthu ambiri amatsatira bodzalo. Poti zonsezi akupanga ma Prophet awawa asing'anga amapanga zomwezi. Ma Prophet anji ongolosera zamaliriro ndi zandale baasi.
@BexSaidi-so8lw
5 күн бұрын
Man of God can l see
@dorothymphaya1829
6 күн бұрын
Bola asakuphenitu in Jesus name
@spargomw
7 күн бұрын
Oyitanidwa nd ambiri koma osankhidwa ndi owelengeka. Ambiri adzafika mdzina langa, nadzanenera, nadzachita zamphamvu kwaotere kadzipatule, says the Lord.
@BrendaKazembe
5 күн бұрын
Ndipo kwambiri Anthu akumalawi samakhulupilira kom odara yemwe akuva mawu kuwachita or yesu amene ananyozedwa Anthu samamukhulupilira km qnakhulupilira kumapeto Kut Ndy mwanad wamulungu
@JaneMoyo-ws2di
7 күн бұрын
Nde munthu opanda chifukwa uzalapa chani mmapempheromo. Poti munthu umalapa chomwe wachimwa
@JONAHMWALUGHALI
5 күн бұрын
i think
@JONAHMWALUGHALI
5 күн бұрын
powerfulwords
@JaneMoyo-ws2di
7 күн бұрын
Otsata ndale anatiuza kale kuti enanso ali pa plot. Nde khosswe ali pa mkhatetu apa Prophecy from God siphonya koma ya Chilima 2025 presidency🙆💔
Пікірлер: 29