Chilungamo chake ndiye ndichakuti chakwera adapha chilima that's all
@dondamissonchdziwe3958
2 күн бұрын
Angoni from south Africa,osangonja,ndizi tsiru za MCP dzi achewa zakupha.Angoni Ndi Wanthu wozi sungira Ulemu Chilima wachita kuphedwa, koma adali Munthu wozi chepesa kumu manga kumunyoza koma iye wosayankhula kanthu mpakana kuphedwa Ndi Chitsiruu Chakwera mbuzi ya munthu pakana khala Kuti nkale,pakada khala chinkhondo chowopsya Ndi A Chewa komanso Angoni tonse takonzeka A Chewa asati zolowere yayi,unkhontho phambili,nkosi kwata ine
@edenngoma8214
2 күн бұрын
Iwe ndiwe chitsiru kwambili . Chifukwa chani ukuphatika achewa ndi MCP . Siyanitsani pakati pa Chipani ndi Achewa . Mapwala ako ndithu
@user-uc1pd1tc2x
2 күн бұрын
@@edenngoma8214mesa big inuyo achewa Ndi apa central Ndipo mumakonda MCP chipani chokuphachi. Ndinkana iyetu watero coz anthu aku Lilongwe mukumaona kuti dziko likuonongeka koma mukumapopabe MCP big. Ndie sizokuti mutukwaneyi onani Malawi wanunkhiramu boss😢😢😢
@edenngoma8214
2 күн бұрын
@@user-uc1pd1tc2x braz koma mwayiwerenga bwinobwino statement yake walemba galu ameneyi ???? Akunyoza achewa kungokhalangati achewa onse ndi a MCP . Chitsiru ameneyi kwambili
@user-uc1pd1tc2x
2 күн бұрын
@@edenngoma8214 Big pakunyoza achewa ndikulakwitsa tisalimbaneyi Ndi Ntundu komano tilimbane ndiulamuliro oipa okuba, okupha ulipowu boss. Apopo basi khululukani ingozisiyani ndithu braz
@FikiriAsani
Күн бұрын
Olira salakwa
@sylvesteralfred8355
Күн бұрын
Zinangovuta nthawi yoti chakwera achoke pampando ndiyomweyi ino, kodi aMalawi tidzachangamuka liti let's all go Kuma Demo pa 10 pano kuchotsa Chakwera ndipo ma Demo amenewa akufunika continueos mpaka atachokapo
@user-sh6gi5uq3l
2 күн бұрын
Many who are encouraging us to take action on this are in the diaspora please let's be careful indeed it hurt and its difficult to bare but let's trade carefully
@user-nx7me7ds5u
3 сағат бұрын
While I understand the concerns about acting,,,it hurts and is difficult to bear, but caution shouldn't be an excuse for inaction,ululu wachuluka ndikusavesa
@wondermsibe1708
2 күн бұрын
Tililimozi SKC moto ambuye ndiwachifundo SKC kufa Ngati galu akulu akulu po mwe ana Gona abwana omwe anati sithila boma mwampavu 💔💔💔💔💔😭😭😭😭
@user-mw3kj4qz7b
2 күн бұрын
For sure we're coming pa 10 enough is enough guys our hearts are bleeding
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
Күн бұрын
I crying Dr Saulosi Claus Chilima tingayiware bwanji,chilima was future for malawi
@fannyzimba149
2 күн бұрын
😭😭😭😭😭koma kulira a mfumu Eeee koma Mulungu yekhayo alowelelepo mwava My Mr Saulos Chilima and all other souls Rest in peace
@PaulKachule
2 күн бұрын
Forever powerful mssg from SKC in my heart, mind Osaopa, Osafooka,osatopa .more fire the Ngoni's Watching from South Africa
@user-gm8gb4bt3c
Күн бұрын
Ngoni from mzimba tili limodzi💥
@frankjolijo
2 күн бұрын
The spirit of Chilima!!....will lead this revolution 🙆🤦🙆🤦🤦😪🥲☀️✨✨✨
@AllanChabwela
2 күн бұрын
Awanso muwamanga???? Zamanyazi iziii mzimu wa chilima uuse mwa ambuye
@gracemaluwa4674
Күн бұрын
Mposo inu
@spargomw
2 күн бұрын
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 Dr SKC and other 8, forever in our hearts 😭😭😭😭😭 Ambuye atonthoze Mitima ya aMalawi😭😭😭😭
@SolomonNjolomole
2 күн бұрын
Kuswakuswa angoni atiphera chilima kumene.
@AishaIshumael
2 күн бұрын
More 🔥 🔥 angoni 🎉🎉
@AnnahJohnson-eb2pw
2 күн бұрын
CHAKWERA MUST GO ✊✊ on the 10th July I will be on the front 😂😂
@frankjolijo
2 күн бұрын
The revolution is now🔥💪✨
@user-gg6uh2wo4x
2 күн бұрын
Am watching from South Africa taking true
@user-si7po9sd5i
2 күн бұрын
Speak without fear, tell the government to understand
@AmosSilumbu-ur4ny
2 күн бұрын
Am feeling very tearful ndkamamva mawu ngat awa okhudza malemu chilima😢😢😢 amalawi tiyen tidzuke pa siku lamademo
@user-do2cs8nf4b
Күн бұрын
Osatopa, osafowoka, tidzafera mbendera SKC mmhh😭😭 ngati bodza ndithu may his soul rest in internal peace, and including the other souls may there soul rest in internal peace😭
Angoni sife zitsiru .one day you will see. Anthu amafika potopa
@FrankZiwoya
2 күн бұрын
Powerful speeches from Ngoni chiefs
@sahwi2020
2 күн бұрын
Painful 😭😭😭😭
@MonicaChirwa-l4b
2 күн бұрын
Well speaking king 😎
@HusseinAdamLidezo
Күн бұрын
Kuyankhula kwa nzeru kwambiri kms continue working hard 💪 👌 👏
@EstherMcheche
2 күн бұрын
Mfumu yalila zosakhala bwino
@user-cf9yz3ei5o
2 күн бұрын
He was a hope. for all malawians especially the youth
@chrispinngaiyaye1401
2 күн бұрын
We need Mafumu olankhula ngati awa! Kulankhula kopanda mantha!
@JohnWanda-og8wr
20 сағат бұрын
Pepan kwambili
@GraceLimani-zw7dx
2 күн бұрын
Ife tamva kuti ago mani agulilidwa nyumba ku 43 ndi mcp ndi azi mfumu wonse amu ntcheu analandira ndalama ma 10 mita zikomo po kumbukila mzimu wa biyeni
@user-uu6ki3nm6m
Күн бұрын
Aaaaaa asithana ndi moyo wa chilima
@natalilungu8487
Күн бұрын
Ndipo infa ya a Chilima yatilizadi kuno zambia. Ndipo ife angoni ndife woliradi. Tingoti pepani amalawi. Mulungu yekha akupukuteni misozi
@user-el8to1te3l
2 күн бұрын
Kuswa kuswa bas madala amwela mazi mwa nkhwiyo awa
@sukiemapemba4094
2 күн бұрын
Tili limodzi angoni zikhale ng'oma ,Moses mkukuyu,chimwendo,nkaka ndi chakwera akufunika zikwanje basi kuphakupha
@EmmanuelGasiten-fo5dr
2 күн бұрын
Gogotu walira uyu, R. I. P BIYENI
@LameckLubani
2 күн бұрын
Am following this all the way from SA
@Hellenistic109
12 сағат бұрын
A Biyeni kuphedwa mwankanza kwambili aaahh 😭😭😭😭💔💔..RIP SKC
Kuthokoza Ngwenyama ife a Saulosi atisiya koma Ambuye ationa ndiponso akudziwa kuti amenewa asiya ana ndi Amai Mary.
@NezBoy-u1t
Күн бұрын
Perfect said chief
@moseskavalo3304
2 күн бұрын
Adaputatu Angoni aziona
@AlexZanda-e5i
2 күн бұрын
Polenii sana amalawi
@Macrina-vv3us
2 күн бұрын
Forever in our hearts Dr SKC
@jeanpetersen5693
Күн бұрын
Ife tikuthokoza kuti timve za mwambo yathu.❤❤
@bridgetmajor3646
Күн бұрын
Osaopa.... Amalawi. 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@DKMWALE-ew3lp
2 күн бұрын
Chiyembekezo chathu
@RabsonMulumbe
2 күн бұрын
May his soul rest in , well int. Peace
@macdulfluhanga6018
Күн бұрын
UTM is just need munthu wamphamvu to lead the party for next year elections.otherwise this is abig campaign. May the soul of SKC rest in peace
@DONNEXKhama-bk1gy
Күн бұрын
Enough is enough aMalawi si ife opusa pa 10 pa nsewu pa vuta
@eliffagondewe8214
2 күн бұрын
😭😭😭Ndipo nde talira amfumu 💔💔💔
@user-lb6ek3ee6d
Күн бұрын
Ndimakhala odandaula kwambiri ndikamaganizira za ifa ya a Chilima mpaka pano zimandivuta kukhulupilira kuti kuti mr SKC anatisiyadi ngati bodza ndinthu
@user-dt4po2kk7o
Күн бұрын
Anthu aku tcheu aphwanya galimoto yimene yinanyamula chilima 😊😊😊😊
@CHESOLO
2 күн бұрын
Apatu nde kuying,arura awudzeni
@IvyMadumuse
2 күн бұрын
Rest well skc
@user-px1rq6sj9t
2 күн бұрын
Angoni atopa
@GiftSimbi-cv6kl
2 күн бұрын
Uyu wadya ndalama koma aja alakhula poyamba paja ngachilungamo
Mulungu akhale mbali yanu a mfumu.osaopa, osafooka
@NEBERTMVULA
2 күн бұрын
CHAKWERA, CHIMWENDO BANDA, KUNKUYU, MKAKA, ZIKHALE NG'OMA, CATHERINE HARA be careful Malwians are watching your footsteps! Be very very careful. MCP is ended!
Angon simuli nokha nafeso chigawo chakumwera tilkulira sidik mia mwina akawina kumpoto koma chikwawa ndi nsanje they should forget olo atapeleka ndalama chotani koma vote ili mumtima😢😢😢😢😢 dziko lino lafika pena
@SheenahMwalabu-iz3pr
Күн бұрын
A Malawi tiyeni tisiye kusankhana mitundu plz kuchoka kwa Chilima ndimitundu yonse yamdziko muno timamukonda Saulos Chilima and mu Utm muli mitundu yonse. Ife tingompempha mulungu kuti mzimu waanthu amenewa usagone koma ugwire ntchito kwaonse omwe anapanga zoipa izi adzafe atalapa. Apatu anthu oipa ndia MCP not achewa, inde mu MCP munachulukadi achewa koma sionse osapota mcp ayi tidziwe kuti zinthu zinasintha, akulu akale ndiomwe amakonda chipani cha mcp chifukwa choti chinachoka pakati ndezosankha sizitithandiza koposa kuthana ndioipawo 😢😢
Пікірлер: 291