Munandisangalasa yomweo chikangawa❤️❤️❤️🇿🇦🇿🇦🇿🇦🇿🇦 osavera Riiimpopo ndi ndimakhala ngati ndataya kofunikila
@user-ky4ce9gb6j
5 күн бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm
@user-do2cs8nf4b
5 күн бұрын
Koma ntanyiwa. Respect to you May the almighty God protect you wherever you will go
@petroszgambo9949
5 күн бұрын
Keep up the good work comrade 💪💪
@BeliLikhola
5 күн бұрын
Ulemu wanu comrade Ntanyiwa.
@user-ti2ct8ts8d
5 күн бұрын
Salute comrade ntanyiwa,we love you and all Limpopo FM
@ImanRashidi-so4oo
5 күн бұрын
Limpopo FM live from south Africa Durban Pietermaritzburg auzeni zoona amenewa
@yusufbakali
5 күн бұрын
Panopa ine ndinasiya kuvela ma redio ena panopa ndili limpopo yokha basi
@mustafailanga2585
5 күн бұрын
Ulemu wanu big mani mmatimvesa kukoma kwambili god bless you all the time ❤❤❤❤❤❤
@bytonalfred5844
5 күн бұрын
Ntanyiwa and your fellow comrades excellent well done, and keep it up for the battle you are fighting for Mw nation
@harrisbanda5891
5 күн бұрын
Ine mchifukwa chake ndinakana ntchito ya usilikali ndiyapolisi coz fans ya madepartiment amenewa ndiyombwambwana kwambiri, zigawenga zaku Israel and Ruanda zikungolowa mdziko mwathu ngat zikulowa mmanyumba mwawo, chomvesa chisoni kwambiri ndichoti asilikali ndi apolisi angoti vyooooo , vyooooo , osapangapo kanthu
@Musa1828-l5d
5 күн бұрын
Dzitsiru
@Musa1828-l5d
5 күн бұрын
Respect bwana Ntanyiwa 🔥🔥🔥
@harrisbanda5891
5 күн бұрын
Agape khombe amandibowa bwanjii eish!, i dont feel good wen i heard names like agape, kumkuyu, chimwendo, chakwela, zikhale, yolamu, vetino phiri, pter kalaya, billy malata, layitoni mangochi, ben longwe too many to mention
@esaMoha-dm4kj
5 күн бұрын
Mtanyiwwa ulemu wanuw mulungu asinkuphasa moyyo wabwinno ndawi sonse I pray for you all the time amalawi tili phamoto 🤲🤲🤲🙏🙏🙏mulungu dalisani Malawi
@Jimmy-m4z
5 күн бұрын
My brother your number one keep it up
@EyobeAyala
5 күн бұрын
Chifukwa iyeyu..akupanga zinthu zomwe south African ikhoza kukwiya nanzo.zomwe zingaikidze miyoyo yanthu ife amalawi pa chiswe😢
Mulungu akuulura chinachilichonso ku dziko langa koma vuto dziko langa linasankha kusamva koma limamva china chake chitachitika...Ambuye athandize Malawi
Amalawi let’s gather together and fight like our fell Kenya’s bakili tv and Limpopo fm thy are doing there parts ife tonse tikutani kapena yathu ija ya Ulemu???
@harrisbanda5891
5 күн бұрын
Not ulemu as such bro, amalawife ndombwambwana kwambiri man, mtanyiwa and bakili muluzi tv alongside bon Kalindo are doing their part for sure
@sharifujoe7633
5 күн бұрын
Guz Malawi ndiwatu if anyone ali okudzidwa ndikulephera kwa Chakwera tiyen paunsewu tonse pa 10 July
Eyetu ameneyo nde mulungu inuyo ngati mukukwanitsa kutseka anthu pakamwa ndindalama ndiomwewo opusa osusuka achina yudasi Ana anjoka inuuuuu Malawi mizimu yambiri ikuzunzika kusowa chisamaliro zinthu zinakwera kuli okalamba Ana amasiye nzipatala kundende ndi anthu onseee mdzikomu ofuna zabwino koma ayi zikuvuta kwacha mwagwetsa mwagwetsanso ma million mukukhonyolera m'matumba mwanu kukhutisa mimba zanu Nde pemphero la olira ovutika Mulungu samalisiya amayankha mwachangu nde anthu ayamba kugwidwawa nchiyambi chowululika zinsisi zanu I'm repeating all most each and every day kuti you will pay one by one I'm not just taking this is prophetic word Mulungu ndiokwiya nanuuuuuu anthu amagazi m'manja inu
@hanifahmponda8711
5 күн бұрын
Kodi agapeyu ndindani nanga tundu wanji wamunthu ku malawi kuno agalu kwabasi ndi MCP yawoyo
@user-xm3zl5cg6x
5 күн бұрын
Ndipo anapa chilima ndi ameneyo lelo chikuza mawu ndi iyeyo aziwona ndithu atule pasi udindo
@kubengovender6996
5 күн бұрын
We need some more teachings brother man !!
@YasinMusa-ym8lp
5 күн бұрын
Achita bwino 😂😂😂arirata😂😂
@RobertLuka-wy9cl
5 күн бұрын
God bless you mr ntanyuwa ❤❤❤
@AlinafeChimoto-pp7wp
5 күн бұрын
Pa 10 akuchoka bas
@SindawaPelekamoyo
5 күн бұрын
Respect to you bro nthanyiwa keep the 🔥 buuuuuu
@philonampha
5 күн бұрын
27:11 ❤❤❤❤❤
@user-vl9se5bl9s
5 күн бұрын
Limpopo FM is number one
@ShafieIdrissah
5 күн бұрын
Chakwera wamupa chilima kuvuna akhale president galu kwabas
@user-yu4np2wq4s
5 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂musandikomole antanyiwa ine lero Koma kulizithuuuu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@user-vb5dh8ip6g
5 күн бұрын
Our channel Malawian channel we love you comrade together with your people ❤❤❤
@MabvutoMichaelPanagona
5 күн бұрын
Bambo mu mtanyiwa ulemu ndi wanu mulungu apitirize kukuyang'anirani
Ife kuno ku South Africa kungochotsedwa chifukwa Cha zomwe akupanga chakwela😢azaona konko ku Malawiko zomwe tizapange
@sulleahmnyimbili1362
5 күн бұрын
Great Job Ntanyiwa
@EdwardMathuwa
5 күн бұрын
Koma a mcp dzikoli ndiye mwalipezelera bwanji pasana panu nonse a mcp ndi masapota anu nonse zitsiru za anthu inu
@user-uc1pd1tc2x
5 күн бұрын
@@EdwardMathuwa Ndipo mbalame zokhazokha
@ZondoChirwa
5 күн бұрын
Ntanyiwa more 🔥🔥🔥🔥🔥 fire
@user-cd4df3vg4y
5 күн бұрын
Ulemu wanu Comrade ❤
@user-uc1pd1tc2x
5 күн бұрын
My channel ❤❤❤
@JefulyPesulo
5 күн бұрын
Mumakwana ntanyiwa
@PatrickMulangala-os4by
5 күн бұрын
Walemphela udindo
@LoveKhobiri
5 күн бұрын
God be with u brother
@philonampha
5 күн бұрын
26:37
@GeorgeChakuamba
5 күн бұрын
Auze zoona a Malawi iwe umakwana ndipo ndimachita kukuika PA Bluetooth kut maneba amve nawo kkkkkk
@SmileMalanda
5 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@user-uc1pd1tc2x
5 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@Pangolinimw
5 күн бұрын
umachita bwino
@EmanMiles
5 күн бұрын
🎉🎉🎉 to Limpopo FM
@marthablessings1314
5 күн бұрын
Inde bwana wathu❤❤❤
@MecyMalothi
4 күн бұрын
Inuyotu mumakwana palibenso
@LatiffKadyamawuseni
5 күн бұрын
Mumakwana ❤
@ChiefJustin-cl8jl
5 күн бұрын
Limpopo fm ❤
@PetroJack
5 күн бұрын
Limpopo ndi katundu uyu😂😂😂😂
@martinaustin-qm9yp
5 күн бұрын
Kkk koma ntanyiwa usazamwalire uzangosowa mumat tsegula maso ndikutichosa khawa ndikavera mtima kut miyaaah
@YasinMusa-ym8lp
5 күн бұрын
Namu bwana mumata ❤
@user-mo5od8cy3n
5 күн бұрын
No matter anyone to hate but the truth i talk.
@harrisbanda5891
5 күн бұрын
South Africa ikangomuphulisa wagule uja basi, walowa mkati mwana wang'ona ameneyu
@Musa1828-l5d
4 күн бұрын
Chakwera pamtumbo pako galu fiti
@JafaliLysani-nb6bq
5 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@PatrickChirwa-cv5cd
5 күн бұрын
Ntanyiwa mwathatu mungonena za security yanu tsopano kusonyeza mantha. Muzikhala ngati Bon Kalindo olo wa Bakili TV amabwera ndi nkhani ndi pfundo. Inu ndiye a DPP angowonongapo ndalama tsopano. Mukunena kuti muliku Botswana koma ma discussion anu onse mukunena kuti ku ku South Africa😂😂
@user-pv9uk6sc3w
5 күн бұрын
Chakwera woyeeeeeee! Mutu waima, ndipo a Malawi tisalole zopusa
@harrisbanda5891
5 күн бұрын
Amuchita bwino kumuthyola msagwadazo on top of dat mapwala ake , atilakwisapo apaa kafucheche ameneyuu eish
Пікірлер: 190