zikomo kwambiri m'bale wanga ndimaganiza ngati ndindekha ndimaganiza choncho..ndikufuna number yake ndimuyankhule mwapadela ndi galu wamunthu uyu ali ndidyela simasewera akuyalutsa chisilamu
@abdulhameed7808
5 күн бұрын
Basi sitilankhula zambili tingokusungirani ulemu Sheikh Anthu.
Munthu angopha anthu inu mukamuyimile , munthu onyoza chisilamuyo inu mukamuyimile angapilile zimenezo ndani Kodi yinu mufuna azakupheleni agogo anu mpamene muzaone? Kuti izi ndizilombo!!!? Aaaaa mwatipsesa mitimatu nsilamu wantundu wanji osadzudzula munthu akupanga zoipa , bwanji simukuyima pa deen ndikulalika chilungamo aaaaa yinu nde mwalalika mophusa bolani abusa aja nawonso yinde anyika koma yinu mwanyanya , Ndipo palibe akutameni kupatula okhawo akulipilani ndalamawo ife ndife asilamu eni eni choipa timadzudzula basi angakhale Allah anamudzudzula ntumiki wake Muhammad ( saw ) sametime atabwera munthu kuzamfutsa koma ntumiki anayang'ana kumbali Alkah pompo pompo anamudzudzura awa ndayani aaaaa musatinyase mwamva
@FarhaazbashaMdoka
3 күн бұрын
Koma ma ayah wa tikugwilitsa ntchito molakwika 😆😆😆😆😆😆👏👏👏👏👏👏
@FarhaazbashaMdoka
3 күн бұрын
Koma ndalamazi guyz tisamale nazo
@udkconsultancy5567
5 күн бұрын
POWERFUL
@HalisonSolomon
5 күн бұрын
SHEIH MWAPALA ULALIKIWANU MUMAFUNA AKUTAMENI A PRESIDENT PALIBE CHANZERU MWAYANKHULAPO APA ALLA WAKE UTIYO ANGAKONDEE NDI ZOMWE AKUCHITA CHAKWERAYO AYI INUSO ALLA AKUONENI
Iwe undithera nthawi ukuwoneka kuti walandila brown envelope
@abbasdamsonamini4888
4 күн бұрын
Naam Ameen thumma Ameen
@user-ky8eq5ek1p
5 күн бұрын
Bodza pakadalipano akuliyamba ndi Chakwelayo
@RobertLuka-wy9cl
5 күн бұрын
Ameen
@shadrackdrums3536
5 күн бұрын
Ulaliki oti sungatingele kumoyo wosatha komaso sungasithe kalikose. Koma anthu akuwombela mmanja. Ulaliki oti mukupanga taget Boni kalindo, Bakili muluzi tv komaso limpopo FM. Ife we are not going to support any usiles speach or teaching like this wadya bamzi shehe.
@user-xd1cm7tm7t
4 күн бұрын
Chemoto ndinu mwandila ma unforp
@HallimaMakwinja
5 күн бұрын
Kodi munthu ameyu ndani alinaye number yake sheikh ameneyo ndimuuze kuipa koononga chipembezo chifukwa chandalama
@HallimaMakwinja
5 күн бұрын
Inu sheikh watu ndithudi si mslamu weniweni awa akuononga chipembezo cha chislamu ndi mbunzi yamunthu
@harrisbanda5891
5 күн бұрын
Iwenso waikila kumbuyo asatana mmalo mowalesa zoipa which means ndiwe kafiir
@JumaMboneka
4 күн бұрын
Aise kaya ukumati mwiniwakowe Malawi chani kuyambila lelo ndakutuluka ndakuona kut ndiwe wamanyi ukuchwmelela zimenezi kut sheh walalikila mwamphavu mphavuzake zilikut machende ako aise pamoz ndisheh akowo iwe wamanyi kwabas
Пікірлер: 156